olo itapezeka ku malawi kuno can you tell anthu,you will keep denying…..
Jakala
9 years ago
I have been District Commissiiner for likoma. I was very surprised that likoma people can manufacture a story and it will spread like bush fire ad if it’s true. Ndi anthu onama mopanda manyazi. Iam not surprised with this false story
Kachirombo akatangobwera maiko ambiri ku Africa adatsutsa amvekere, “Mphekeserayo si yoona.” cholinga, to maintain tourist friendliness of their countries at the expense their citizen’s lives. Madzi atafika mkhosi amvekere, “Tikutha kuno ehh!” Maiko ndi mabungwe othandiza ali busy kuthandiza Uganda amene sanachite nawo chibwana cha mchombo lende ngati cha madotolo a ku Nkhatabay.
ILALA SHIP DOES NOT CALL AT COBUE IN MOZAMBIQUE AND M.V. CHAMBO OF MOZAMBIQUE OPERATED BY MALAWI SHIPPING COMPANY IS NOT SAILING SHE IS AT MONKEY-BAY GOING UNDER REPAIRS. THE VESSEL WHICH IS OPERATING ON THE LAKE IS THE NEW SHIP M.V. CHILEMBWE OF MALAWI SHIPPING COMPANY[MOTA ENGIL].
PLEASE NYASA TIMES AND ZODIAK FIND OUT WHAT MODE OF TRANSPORT THEY USED ,IS IT BOAT OR SHIP, ALSO NAME OF THE SHIP, AND HOW THEY MOVED FROM COBUE TO MALAWI. [?????????????????]
Tiuzeni zoona zoti timve anthufe ngati ebola yapezeka kapena ayi
olo itapezeka ku malawi kuno can you tell anthu,you will keep denying…..
I have been District Commissiiner for likoma. I was very surprised that likoma people can manufacture a story and it will spread like bush fire ad if it’s true. Ndi anthu onama mopanda manyazi. Iam not surprised with this false story
Be serious plz dis z nt malaria.
A malawi asatipindire ndevu nkamwa, utsi sungayake popanda moto.. EBOLA YAFIKADI.
Kachirombo akatangobwera maiko ambiri ku Africa adatsutsa amvekere, “Mphekeserayo si yoona.” cholinga, to maintain tourist friendliness of their countries at the expense their citizen’s lives. Madzi atafika mkhosi amvekere, “Tikutha kuno ehh!” Maiko ndi mabungwe othandiza ali busy kuthandiza Uganda amene sanachite nawo chibwana cha mchombo lende ngati cha madotolo a ku Nkhatabay.
chitaponi kanthu zapa nkhotakota chifukwa a mozambique ambili amatsikila pamenepo
Ebola ndikanyama kanji?kumafufuza kaye bwino pamapeto ake kumalengeza A ZBS timakudalirani mwatani kodi awulusi enawa ayenera kuwachotsa masengo(MALUNDANI BOY SANTU)
ILALA SHIP DOES NOT CALL AT COBUE IN MOZAMBIQUE AND M.V. CHAMBO OF MOZAMBIQUE OPERATED BY MALAWI SHIPPING COMPANY IS NOT SAILING SHE IS AT MONKEY-BAY GOING UNDER REPAIRS. THE VESSEL WHICH IS OPERATING ON THE LAKE IS THE NEW SHIP M.V. CHILEMBWE OF MALAWI SHIPPING COMPANY[MOTA ENGIL].
PLEASE NYASA TIMES AND ZODIAK FIND OUT WHAT MODE OF TRANSPORT THEY USED ,IS IT BOAT OR SHIP, ALSO NAME OF THE SHIP, AND HOW THEY MOVED FROM COBUE TO MALAWI. [?????????????????]
kdi anadwala chiyani?