Email a copy of 'Malawi govt insists no fees in primary schools' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

15 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ALOSWEA
8 years ago

Penapake mafunso akumandivuta ,udido wa Boma ndi uti tsopano,my tax mayoOoooo!!!!!!

Wilson Banda
Wilson Banda
8 years ago

pempho langa mukamakambirana za fees ya primary muziganizila makolo omwe akusunga ana achuluka kaamba kamavuto osiyanasiyana,pomwepo pali asecondary ndi primary.osewo akudikira thandizo monga kudya,kusamba,kuvala,maphuziro ndizina zambiri chonde aganizileni makolo amenewa primary yokha isiyeni chomwechi.

Ernest Kuliyani
8 years ago

school fees can encourage school dropout

Yohane Lupenga
8 years ago

Nzomveka bwino. Koma ngati boma yalamula ku maphunziro a pulaimare ndi awulere nanga dzina la ‘school fund’ ikuchokeranso kuti? Kodi sinjira yobisalirapo kuti ana adzilipila mwa chinsisi? Maphunziro a ana ambiri akulephera kuyenda bwino maka amasiye ndi ovutika kamba kadzina limeneli ‘school fund’ mafumu,makhansala,akomiti ndi a phunzitsi apeza njira yodyera. Koma akuvutika ndani mwana wa masiye ndi wovutika ngati alibe ‘school fund’ imeneyi sakuloredwa kulembedwa mkaundula wa sukulu,kulowa mkalasi ndi kulemba mayeso. Kodi tsogolo la mwanayi, la dera ndi la dziko zikukonzedwa? Bwanji pakhale njira ina yopangira source ‘school fund’ like school garden,expressive art, variety show, zone competition of different… Read more »

iwe
iwe
8 years ago

Malawi yatha Ngati katani apa dziko lukanika kuyendetsa mpira ukanikaso

Joe
Joe
8 years ago

Just introduce a standard and affordable fee so that ministry of education can purchase good learning materials for the pupils. One can’t get something from nothing.

chatonda
chatonda
8 years ago

Ministry of Education, what are you doing with Chichiri secondary school teachers who do not teach but do part time and even create their own school just next door?

sapitwa
sapitwa
8 years ago

Ife kale timalipira 15 Shillings nthawi zina zikavuta timatha kulipira Madzira a nkhuku. If you defaulted paying school fees, you were sent back home. We were in turn getting keen interest from parents to check what we had learned every day. This was because they felt the pain in paying school fees and would want to see what the fees was yielding. We were getting good education because Teachers were also being checked by parents. Sukulu ya ulere si solution yothetsa umbuli infact mbuli zachuluka masiku ano chifukwa cha sukulu yaulereyi. Ma graduates a lero akulephera kulankhula chingerezi chokazingika bwino… Read more »

Mnunkhaludzu
Mnunkhaludzu
8 years ago

The Government full of mapwevupwevu. Reversing key decisions already made is a sign of failure and incompetence. You need to listen and make proper consultations with the people….Zakanika apa basi!

chenkute
8 years ago

Hu kimano mukamapanga ma program anuwa muzipanga mwanzeru chifukws2 APA tikuona kuti palibe ndi chanzelu chomwe chikuchitika .mutati muone ma iko anzanu mupeza kuti mwana was class 2 olo 3 primary akuchikulumula chingelezi komano kwathuko munthu was form four akulephe kulankhula . muzifunse kuti chifukwa chani?

Read previous post:
Airtel donates medicine worth K2.4m to Zomba district

Airtel Malawi has come to the rescue of Zomba people with a donation of 54 cartons of medicine and other...

Close