Email a copy of 'Malawi govt MPs celebrate K500mil cut on education budget' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi govt MPs celebrate K500mil cut on education budget' to a friend
Cash strapped Lilongwe City Council says it has hired a professional debt collecting firm in a bid to recover K86...
Our leaders are out of touch. This is dangerous.
AFTERALL KWATHU KU EASTERN REGION TILIBE NAZO NTCHITO ZA EJUKWESHONI YANUYO, MUNTHU UMADYA EJUKWESHONI? EH? KU MTL, MATHANYULA AFTER KA MTELA KA GONDOLOSI BASI KWACHA KUDANSO, KUMA GAME LIZEVU KUMPOTOKU NDIYE UKU NDIYE EH MWAWAPWETEKA.
UKU TIMATI KUCHEPETSA MIKANDA MCHIUNO!!!
Its true. Ku education nde kwachuluka cash gate. Ndalama zomwe zimaperekedwa ndi zambiri koma mukaone komwe zimathera. Umphawi mma school ukupitabe patsogolo. Ana akulipira akuti development fund. Mwana kuti amuphunzitse bwino akuti azipanga part time. Koma kaoneni kwa a Dem wa accounts akugula galimoto zodula, kumanga nyumba za pamwamba mphunzitsi akukanika chonsecho iyeyo grade yake ndi yayingono (m) kuposa mphunzitsi aliyense. Azichepetsedi chifukwa ndalamazo zimangothera mmatumba a anthu a ku office.
Hon Patricia Kaliati was a teacher herself. why can’t she school her friends that education allocation does not necessarily need a cut, but an increase. its really an insult to Malawians especially us our sons and daughters are doing school in Community Day Secondary Schools in villages. shame being a Malawian
Oh dear – everyone knows education is the route out of poverty – it’s not rocket science
I wish the government side should go out to see for themself what is actually happening on the ground. If they aré real malawians the would have to celebrate the cut. Shame on the for the celebration.
The celebration was for defeating the vocal opposition and not otherwise. Inu simukuona pamenepa?
sad but this old man from mzimba haaaaa!watondeka resign man
mbuli
ana awo amaphunzira kunja ,ndalivomereza bible langa,adzakhala odzikonda.