Email a copy of 'Malawi govt refuses to fund forensic audit on voter biometric kit' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi govt refuses to fund forensic audit on voter biometric kit' to a friend
The main opposition Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera is courting the UTM party led by Vice-president Saulos Chilima...
Not only that Dear Linda, but also used for funding the stupid cadets, Does it come under budget line? Bodza la mkunkhuniza lopanda nalo manyazi!
Che Henry Mussa, Musaname Kuti Governmemt Can Never Jump In And Say It Will Fund The Audit Because It Operates Under Budget Line. How Did You Jump At Funding The Appeal To Block UTM Registration? Was It Under Budget Line? Mukunamiza Ana Eti? Manyazi Mulibe, Mmaso Muli Gwaaa Ngati Mfiti? Kukana Kali Kutsaya? Mwagwidwatu Kale Apa Mutabisala Mmbatata! Gogo Wanuyo Akupatsani Chiyani Apa Muli Nkhope Ngati Nyani? Mxiew!
It’s obvious, ain’t it? DPP cannot authorise funding for an investigation which will reveal their clandestine strategy to rig. They would have authorized if the audit were on opposition, particularly MCP.
WHERE IS BAKER TILLY FORENSIC AUDIT REPORT UP TO DATE ?
TO HELL WITH YOUR AUDIT REPORTS —
Asaaaaah. koma abale.chimatchini chipezeka bwanji ku mazambiki. Munenatu bwino inu.ngati inali deal eeeeeh am very sorry Mulungu waiona ndipo achitapo kanthu. Kuti mudziwe kuti kulira kulibe msinkhu,mkulu woyendetsa chisankho analira kkkkkkk nde be careful
Mulowererepo ambuye,ife anthu osauka amene tilipo ambiri miyoyo yathu ili pa ngozi.Anthuwa amangotifuna pa mavoti basi .GOD REMEMBER MALAWI
Kodi ma polls akenena kuti DPP idzawinawa simukuwamva? Mukufuna anene kuti bwanji. Did they say DPP ikadzabela idzawina? Tazimvani kamodzi relatives (abale)
for your own information palibe cha new one chilichose angabwelese peter mutalika basi kungonama miseu basi antu mufele zimenezo
a musa inuyo nde mukufuna muzioneka ngati a shasha inuyo wopanda nzeru ngati iwe , basi inu mungobela movoti basi antu akusiyeni , you just want to exploit our votes on a voting day siziteka zimenezo mutalika wakalamba sangalowe pampando kawili pa mavoti okuba that’s nonses, stupid Malawians mumanama kuti independence inabwela timazilamulila pali chani pamenepa aziba mavoti two times inu muli momo mukungokala for nothing
No surprise there, why would they want to fund their own guilty verdict?