Email a copy of 'Malawi Kwacha appreciation manipulated: Chakwera blasts Mutharka’s zero economic common sense' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

78 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Phodogoma
Phodogoma
8 years ago

Leader of opposition why are you wasting time over economy of Malawi being manipulated. Do you know Gondwe? He is an economist who was recogized by world bank where the man was holding the highest with 50 white economists as his juniors. Gondwe understands the economic concepts better than anybody else. Remember for Bingu to tick it was due to Gondwe. Now Gondwe is just registering his economic tricks. Let him handle Malawi economy again. If Malawi gains its economy back to its expectation as it was during Bingu, then Chanco or Poly should recognize this old man Gondwe.He mus… Read more »

Phodogoma
Phodogoma
8 years ago

Wopenga si Chakwera yekha ayi. Mulipo ambiri ngakhale iwenso Denguzman ndiwe wa ziwala m’maso ngati ankulo ako Abraham. Kukwera kwa mtengo wa mafuta sizikhuzana ndi chuma chaziko. Ngati dziko limakhala losakweza mtengo wamafuta pamene mtengo wamafuta wakwera padziko lonse ndiye kuti dzikolo sikugwiritsa ntchito automatic fuel pricing. Panopa fuel wakwera padziko lapansi. No way Malawi can survive with automatic fuel pricing mechanism without instant adjustment. Ndipo ngati Abraham angakhalankhule mopusa ngati m’mene walankhuliramo ndiye kuti Abraham ndiopengetsetsa zedi. Iweyo ndi Abrahamyo mukuona ngati a IMF aja ayamba kupereka ngongole ndi zithandizo aja ndi oputsa. Iweyo ndi Abraham wakoyo ndiye kuti… Read more »

Denguzman.
8 years ago

Amalawi, bwanji fufuzi zina zikumayankha ma comment ena oputsa against Chakwera. Mwina anthu ena simumatha kutsiyanitsa nkhani zandale ndi nkhani zokomera mtundu wa Malawi. Speech ya a Chakwera siyandale, inetu sindine wandale koma zandale ndi madzitsatira bwino. Zanazanali a Chakwera anena ku ndalama yathu ya kwacha siikuyenda bwino enanu mukuti Chakwera ndi wopenga. Lero pa 8th May fuel wakwera mtengo, nanga pakati pa Chakwera ndi boma ndindani amene akuuza mtundu wa Malawi zoona. Tikamatengera kutsangalatsa a President mu zinthu zoputsa dziko lathu silidzapita patsogolo.

Makaiko
8 years ago
Reply to  Denguzman.

Wopusa kwambiri iwe matako ako mbuzi

Denguzman.
8 years ago

Amalawi, bwanji fufuzi zina zikumayankha ma comment ena oputsa against Chakwera. Mwina anthu ena simumatha kutsiyanitsa nkhani zandale ndi nkhani zokomera mtundu wa Malawi. Speech ya a Chakwera siyandale, inetu sindine wandale koma zandale ndi madzitsatira bwino. Zanazanali a Chakwera anena ku ndalama yathu ya kwacha siikuyenda bwino enanu mukuti Chakwera ndi wopenga. Lero pa 8th May fuel wakwera mtengo, nanga pakati pa Chakwera ndi boma ndindani amene akuuza mtundu wa Malawi zoona. Tikamatengera kutsangalatsa a President mu zinthu zoputsa dziko lathu silidzapita patsogolo, kwainu amene ma sapota a DPP choti mudziwe ndi ichi kunjaku a Malawi akuwona.

Denguzman.
8 years ago

Amalawi, bwanji fufuzi zina zikumayankha ma comment ena oputsa against Chakwera. Mwina anthu ena simumatha kutsiyanitsa nkhani zandale ndi nkhani zokomera mtundu wa Malawi. Speech ya a Chakwera siyandale, inetu sindine wandale koma zandale ndi madzitsatira bwino. Zanazanali a Chakwera anena ku ndalama yathu ya kwacha siikuyenda bwino enanu mukuti Chakwera ndi wopenga. Lero pa 8th May fuel wakwera mtengo, nanga pakati pa Chakwera ndi boma ndindani amene akuuza mtundu wa Malawi zoona. Tikamatengera kutsangalatsa a President mu zinthu zoputsa dziko lathu silidzapita patsogolo, kwainu amene ma sapota a DPP muzipenya kutsogolo osamakomedwa ndi zinthu zopanda pake coz kunjaku a… Read more »

mlomwe2
mlomwe2
8 years ago

WHICH INDICATORS CAN SHOW THAT KWACHA IS APPRECIATING????????????????????????????? PLEASE TELL ME. THERE IS SENSE IN CHAKWERA’S ARGUMENT.

Nyifwa-Ilenga
Nyifwa-Ilenga
8 years ago
Reply to  mlomwe2

In all what peter said it is untrue that it can be 100% false. At least a 0.001% was to be awarded.

Truth pains, yes.
8 years ago

Malawi has been waiting for a such polite leader of opposition, bringing out facts and backing points not rubber stamping and praisings, Chakwera has hinted and EAM has agreed to Chakwera`s facts. DPP should not think that we are all sleeping, we are watching, we all know that some notable gurus paid huge billions to make kwacha look appreciating, we all know that, cheap politics to gain confidence will not work this time, you cheated the elections yes, but this time you will not cheat again, bravo Chakwera, bravo opposition, we will fight until you will be mad again like… Read more »

chindele chakufikapo
chindele chakufikapo
8 years ago

The day will come when the north will rejoice.the seeds of segregation which you sowing will not gereminate at that time. Proud northener.com

Kondwani
Kondwani
8 years ago

Chakwera usadzapangenso mistake yotenga running mate wakumpoto. Bwezitu uli president lero pachipanda mistake imeneija. Take a southrner udzawina 2019.

supportorwaDpp
supportorwaDpp
8 years ago

Akulu chimene mungadziwe ndi U president antha kukhala wina aliyense; Onse amene akhala u Prsident muno M’malawi muno sitimadziwa kuti atha kukhala a puluzident; Siyani kunyoza; Ndani amadziwa kuti Joyce angakhale President no body; Komanso mukamalakhula mudzimizera malovu osatha mau, Lero lomwe Fuel Wakwera IS that not a sign kuti ndalama yathu yagwa? Ndiye mudziti akunama bwanji wosavomera mau akakhala wokoma, Promisory Note Chuka Sanalembebe mpakana pano amuuza ndani wo posa Secretary Ku Treasury, Amangwetu be very Careful; Dzikoli pakali pano likulamulidwa ndi Crooks oti antha kutuma kukampha Alibino omwewo mkukhala woyambirira kukapepesa msanga ndikulira kwambirikwambiri mfiti imatero, Komanso anthu… Read more »

Read previous post:
NICE uses sports to disseminate HIV/Aids messages to masses in Mangochi

The National Initiative for Civic Education (NICE) Trust says football can be used as a medium to disseminate HIV/Aids messages...

Close