Email a copy of 'Malawi leader kicks out spokesman: Timpuza was drawing two salaries' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi leader kicks out spokesman: Timpuza was drawing two salaries' to a friend
CCAP Blantyre City Presbytery has donated 64 life straws worth K720 000 to Chimwankhunda disaster victims on Sunday. Almost 64...
Salarygate odala kkkk
Okanidwa ndiwokanidwa basi
Shaaaa lelo pa 40 February 2015…..zoopsa
Money is the root of all evil and man needs roots!
Koma iyayi asaaaa oweeee
Peter mutu wake sugwira,nde ampezaso kt wina ngat timpuza??kmaso olakwitsa ndi a MBC pomupatsa ndalamazo osat iyeyo…….nde apitala ganizani ngat munavayapo pa khomo la school
anapisa mthumba ndani?amadzipangira yekha salary ngati,ayi opusa ndiomwe amampatsa muwafufuze bwino amenewo ndiye mbava
pa MBC nde paola, imagine ma pronotion kumangopatsana mosaona ma qualifications amunthu, azimayi kuvulidwa ndi ma Directors & Controllers a sevethday – (enanso ma pepala awo ochepa) a seventhday – akuziziwa. Ma secretaries kuvulidwa kuti naonso akhale ndi mphamvu ngati bwana, ena mma dptmnts akuvulidwanso mosamveredwa chisoni kuti kunyumba asiya azimuna awo uh uh mavuto alipo. It is only at MBC that when one hold a diploma or MsCE he/she can be elevated to a Controller or Director. Che Nankhumwa nanu mwayamba kuononga office yanu kuyamaba kupanga promote mlamu wanu Regina Chimenya yemwe alibe mapepala oyenelera kumuuntha from Grade 9… Read more »
Mchiyani Kodi A Malawi?
Mwasambo is not accountable for that,was he stealing or getting paid?