Email a copy of 'Malawi man, 47 gets 12 years jail term for sexual assault' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Brainfast Mpoto
9 years ago

Amakhoti phulizi mabwana tagwira mwendo yanu.tamamasulirani bwino malamulowo.ine yimeneyo nayina ngati rape case,ndiye 12yrs yachoka kuti mmalomwa life imprisonment?mthakuona difference ya 40yrs,unsounded mind.otsamayang’ana nkhope nyani kuphakwaketu.

Munnyabu
Munnyabu
9 years ago

Its my prayer tht this was his first evil act on this child with good medical treatment who knws there is stil hope tht she may be negative. Bt why, when u knw very wel tht u r HIV + why intetionaly infect innocent souls her? Suppose was ur child how would u feel? A malawi let us be civilised God is watching

kadamanja
9 years ago
Reply to  Munnyabu

Am shading tears, why???? Government should do something here on these MONSTERS. FUCK! Kaliat where are you?

godobaman
godobaman
9 years ago

mwanayotu koma wafika pandiwo ndithu ayenera kudyedwa ndithu 12 years kumakhala kuti mafuta akuwoneka ntuluseni munthuyo

Inu
Inu
9 years ago
Reply to  godobaman

Are you serious??? If you have nothing to comment why not just keep quiet. I cannot expect that you are of any value to Malawi or indeed the world. I wish there was a way to send guys like you to Mars

buthi
buthi
9 years ago

Nanunso aMlomwe , mwanayotu ndi wa 7 yrs ndizomwe mukukamba apa zamavalidwe sizikugwilizana

Wezi
Wezi
9 years ago

Kodi abale, ana akaziwa tidziwaveka mapant azitsulo kodi? Nkumatenga makey wo?

innocent
9 years ago

just give him Death sentence bola

zumbwanga
9 years ago

abale kukwimila bwanji? Panopa akazi ndi ambiri ofuna banja osapeza bwanji?fyn sukufuna ku kwatira mahule ali mbwee kutapa kutaya.

buhle mkwananzi
buhle mkwananzi
9 years ago

bola 12 yo si za ma 6 zija abale, mwana wa mkazitu akuzunzika pa malawi pano!!!!!

Dry Cleaner
9 years ago

koma oba ma millions a boma,umbonso ulipo okwanila ,misonkho ya anthu ambirimbiri,ndalama imeneyi ikanathandiza miyoyo yambiri zedi kuchipatala, akuti ayi koma 3 years.koma iyi panda umboni okwanila,mwinaso Theu to ndi openga,mukuti 12 years. ma judge athu koma ali ndi mizimu ????

cynk
cynk
9 years ago

God forbide zoona kumachita kunena monyadira utatambasula mapwala akowo kuti uli HIV postive wapha mwana waeni. ukafere ku ndende konko, akazi kwatirani ndi mphongo ina

Read previous post:
FND asks Malawi govt to release ‘official names’ in Cashgate report and pursue K92bn graft

One of the vocal civil society groupings, the Forum for National Development (FND) says the Democratic Progressive Party (DPP) led-government...

Close