Email a copy of 'Malawi media increases civic education on Information Bill' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi media increases civic education on Information Bill' to a friend
Call boys in Mzuzu City have been given up to April 1 to leave bus terminals or face arrest following...
akukani Access to Information Bill chifukwa chani? ndie kuti akudziwa ikapangidwa pass mu parliament, adzayaluka chifukwa cha cashgate ya 570 billion ija ndie kuti idzawaika poyera kuti anasolola ndi iwo osati JB. Ife tatopa nkutibera and we demand that government should take the undoctored Access to Information Bill to parliament and have it passed into a law. Kodi mesa munkatiuza kuti tikakuvoterani mudzapanga pass bill yi? ndie lero chikuvuta ndichani kuti mukwaniritse malonjezo anu?
Good move,anthu adziwe zoona zake