Email a copy of 'Malawi men ‘developing breasts’: New ARV side effects' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi men ‘developing breasts’: New ARV side effects' to a friend
Che Nkope comic-maker Nicholas Mbonera, who is also a DJ at Malawi Institute of Journalism (MIJ) FM, has given his first...
Masiku ostsiriza
Zandikhuza zedi,Mulungu chonde mankhwalawo ndinu munalowa mmitu ya akatswiri nkupeza ma arv kuti tisathe apo tikuthokoza chifukwa munatikonda monga muja munatitumizira mwana wanu yekhayo,tikhululukileni tizingomwa mankhwalawo koma zayambikazi Ambuye simulephera zisapitirire,tagonja anzathu munauza kuti aziyangana njoka ya nkuwa atakuchimwilani koma chifundo chanu chopambana sanapitirire kufa ifenso tikumwa ma arv tili ndi moyo koma Ambuye sitinanve kuti ataona njoka ya mkuwa sanadwalenso ai,Ambuye chonde chonde tagonja tapemha talapa tithandizeni.
People who have not walked the corridors of a medical college are very difficult to handle,they do not understand medicine.Every drug has its own side effects,and we respond to drugs differently.Even Asprin has adverse side effects,and some people have been told not to take asprin,the same applies to HAART,others are on 5A and some people are on 7A,why because of the way their bodies reacted to that particular regimen,fotseki.
Iwe Balaka guy, yu think being in the corridors of medical colleges nde kuti wamaliza ma sewera. Yu cannot know everything simply bcoz yuv bn in medical corridors. Matama bwanji. Think twice if not thrice bfo yu comment. Chonsecho unalowera likasa/cheating
KUSAMVA KWATHUKU TIMERA ZOMERAMERA CHAKA CHINO ndiiithu.
amalawi kusanva kumangoti kuphunzila mmitu muli gwa mwaiwala kunabwelanso mankhwala ena a cancer ndi madolo omwewo munaliala nawo kuti chwe ,kenako ena waja anthu amaoneka ngati ma baunsa inu tizipemphela chonde,koma kukabwela wopempheletsa ndiye kumunyoza muli ndi wa ku madzi mukhala choncho
this is already stipulated in the Malawi clinical guidelines for the management of HIV/AIDS in adults and children, that regimen 3, 4 and 5 that contains EFV( effavirens) has got the side effect of breast enlargement(gynacomastia) in children and men. and usually when this happens you have to change to NVP( niverapine) even though it written that the breast enlargement resolves spontaneously. So tell the people the truth rather saying you need research. This should not be news because we already know this would happen.
MANKHWALAWO ABWELERE KOMWE ADACHOKELA. KUNO SIKOYESELA MANKHWALA AI.
I dont understand azimayi bwanji
sakupezeka ndi ma side effect do
you mean ayamba kumela ndevu
ma canadian asatinamize
Please in situations like these,avoid showing the persons face. If told and accepted, its OK.
By the way where is the noise about Mdulidwe now.
Ooo arv please lets stop intercourse. Though sex is the no 1 intertainment on earth.