The last day events,believe it or not,there is no any other explanation. 2much false prophets in the country,they didn’t even foresaw the impending calamity,busy prophesying about who is gonna win the elections za ziiiii,foresake.
Gimbogo
9 years ago
Pitala atsogokelere mtundu wa a Malawi popempheleramvula yasaononga katundu ndi anthu abvule zobvala zake ndikubvala saka ndipo akagudumuke paphulusa ku Ndata kwa masiku asanu ndi awiri
I thought you, the same people, yes you Malawians prayed for the rains to god, didn’t you pray for the amount?? Kkkkkk gullible creatures. you even boasted good had heard your prayers, today mukuti Malawi watemberedwa, jesus akuchitileni Chifundo, do you know wat you want?? when you are praying , do you know to whom you are praying?? dho you believe that God hears every prayer of all people in the world without limits??
DPP must repent their sins. After, zonse zitha. bible says if my pipo who r called by my name will humble themselves n pray n turn from their wicked ways then shall I hear from heaven .
Patriot
9 years ago
Mvula iyi ikubwera chifukwa cha ujayu. Pulizi a Mvula, a Kusefukira ndi a Ziphaliwali, pitani ku Ndata kumene kumkhala mkulu wabweretsa miliriyi.
True patriot
9 years ago
God saved the Israelites in the wilderness,and can not let his people suffer anymore.It will be well in God’s name.
zonsezi ndichifukwa chobera mavoti pitala tinkanena munthuyi ndi wakumidima kutereku akulipira mwazi umene adalonjeza kuti akamuwinitsa alipira. utenge anthu aku mwera kwako komweko kuno ayi
The last day events,believe it or not,there is no any other explanation. 2much false prophets in the country,they didn’t even foresaw the impending calamity,busy prophesying about who is gonna win the elections za ziiiii,foresake.
Pitala atsogokelere mtundu wa a Malawi popempheleramvula yasaononga katundu ndi anthu abvule zobvala zake ndikubvala saka ndipo akagudumuke paphulusa ku Ndata kwa masiku asanu ndi awiri
I thought you, the same people, yes you Malawians prayed for the rains to god, didn’t you pray for the amount?? Kkkkkk gullible creatures. you even boasted good had heard your prayers, today mukuti Malawi watemberedwa, jesus akuchitileni Chifundo, do you know wat you want?? when you are praying , do you know to whom you are praying?? dho you believe that God hears every prayer of all people in the world without limits??
a yehova abale amene atisiya akwana tatisunguleni life yathuyu tilerere anawu, sanakuleyi.
In jesus name,
pavuta apa