Email a copy of 'Malawi Muslim body hails APM’s leadership style' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

38 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
NYAKWAWA
9 years ago

Good leadership pamene mu cabinet ya anthu 20 muli akhristu= 18, asilamu =2. Ma ambassador 8 omwe wasankha akhristu=8 asilamu=0 Nthumwi 68 zomwe wanapita nazo ku USA akhristu=65 asilamu=3 ma advisor omwe asankhidwa 10 akhristu=9 asilamu=1 Top 10 DPP NGC positions akhristu=10 asilamu=0 12 recently appointed top civil servants akhristu=12 asilamu=0 palibe asilamu ali ndi ma degree amene akufunikawo? do you call it good leadership style pamene ife asilamu tikuponderezedwa? Ma northerners akamaliza motion ya federalism, ife asilamu tibweretsa motion ya religionism kuti mukamasankha maudindo ndi mipando ya m’boma pazikhala atleast 40% allocation to muslims in every category bkoz malawi… Read more »

Chinyama Phiri
9 years ago

Asilamu munthu olamulira bwino amamudziwa? Hehehehe! Chikwangwala chamuthu ichi

Kangandiwamba
Kangandiwamba
9 years ago

Thats the leader malawi has been waiting for

A hunter is not a soldier

@John 2019 amako akamazapanga kampeni uzizawerenga onse obwera pamisonkhano pawo ndipo manambala ake uzawapatse a mec kuti azawerenge ndipo amakowo azawina apo bii mukhalira kupempha ma lecture kunja ncholinga tiziti she is a most poerful woman in africa kkkkkkkk mwagwa nayo!

Mamwene
Mamwene
9 years ago

@ No. 9, (Frank) Ilipo nduna ya chisilamu and a devout one for that matter. Austin Atupele Muluzi, MP for Machinga north. He is Minister of Energy, Mining and Natural resources in Prof. Arthur Peter Mutharika Administration!!!!!!

Dusy
Dusy
9 years ago

Iwe Jones Chavula let me correct u idiot Uladi Mussa is not a Yao but a chewa by tribe with an Islamic faith kuchokera kwa makolo ake Ku salima.Iweyo mtumbuka utha kukhalanso Moslem osakhalanso mu Yao which means every Moslem is not a Yao.

Jabulosi
9 years ago

Shallow Thinking Boko Harams, Just because Muluzi is a moslem!!!shah! Why back Thieves?????

KK
KK
9 years ago

Munthu opusa, ombwambwana, ofoyila, ogodomala amabeledwa kumene nanga tulo lili mmaso ndiye asabeledwe? Pa tauni pamafunika kuchangamuka. Osati tulo mpaso thoo! monga mmene amchitila atsogoleri anuwo.

Imraan Sadick
9 years ago

Nothing but the truth `zikumpweteka adzimangilire!

George Lihoma.
George Lihoma.
9 years ago

He will go down in Malawian History as the first President to win from opposition and the other as the first president to loose while in power. Do you realise what difference this means?
By the way, paja campaign inakula ndi mawu achilimbikitso kuti BOMA SILILUZA.

Aliyense ali ndi nthawi yake. Whether we want that reality or not but its the normal truth.

Changers
Changers
9 years ago
Reply to  George Lihoma.

Was Muluzi already in government when he won an election? And was Dr. Banda not in Government when he lost an Election? Some of these accolades are a sign of desperacy

Read previous post:
Mutharika’s speech during commemoration of Police National day: Full text

It is with great pleasure and profound happiness that I stand here this morning to celebrate the 93rd  anniversary of...

Close