Email a copy of 'Malawi Muslims against law limiting children per family' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

42 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
jomo
9 years ago

Let’s be honest on commenting issues not because u hate certain group of people then u comment kaka! Read the whole story and u find kuti nawoso a Roman catholic akutsutsanazo so why u just criticizing one group? That’s why we Malawians we still stupid cause we tend to give away our values to westerners

mose kez
9 years ago

kupusa kwa mulungu kupambana kuchenjera kwa anthu, mulungu sanganene kuti mubelekane ngati mchenga asakuziwa chimene chigachiti ku sogolo, chimene chazaza mumitimayathu ndimwano kuoneka anzelu pomwe zelu. gonjani pamaso pamulungu ndipo iye azakukwezani umeneo ndimwano waukulu pamaso pa mulungu. lamulo ili likanabwera 1920 bwenzi uliko iwe ufuna kuwasekeleza azako kuti asabadwe lemekezani pakukwanisa cholinga ndi chifunilo chake

Richard Pankomera
9 years ago

Moslims are on track none can limit number of children to one’s choice. Ulesi ndumene wakula if you say anthu amenewa kuchipinda ndikumene amakukhulupirira do you want to tell me that you don’t have bedrooms in your houses? Komakuberekeraanakwina

fletcer
fletcer
9 years ago

thats a good law considering the land that our country has not what so called coran or what so ever name u call says.

mopia
mopia
9 years ago

Umbuli basi. This is not an Islamic state. Afterall what influence Muslims (13%) have? This is the most imporant law that Christians will 100% support. Check Parliament records as to how many Muslims MPs do we have. Can they disturb a quorum as required?

kadamanja
9 years ago

Mtundu umenewu aaaa! kukonda kuchinda basi sukulu inawakanika anthuwa, anzathu mayiko akunja asilamu womwemo amabereka ana wochepa iwo akukana chani? kupusa chisilamu chake chiti? Lamulo ligwire ntchito basi. ndichifukwa chake anzathu kumpoto ndi pakati akufuna fedulo. Ngati sakufuna achoke basi. Kubeleka ngati anzanu satha Kuchinda! zina izi mwanyanya. I think federalism will help to control the population.

kassim mahomedi
kassim mahomedi
9 years ago

a satanic ndi amene amayika malamulo oti anthu azikhala ndi limit pobeleka chifukwa mulungu mu bible olo quran sanaike limit za limit zikuchokera ku USA KUMENE SATANIC YATENGA MALO ,ANTHU AMENE AMAGANIZA ZOTI NDI ANZERU KUPOSA MULUNGU ZITSIRU ZIMENE ZIKUTIBWERETSERA U GAY KU MALAWI AKAPANDA KUTERO NDI SANCTION. SATANIC YABWERA MUFUNE MUSAFUNE

Mkalapwaga
Mkalapwaga
9 years ago

The issue is not about huge population but allocation of resources in this Republic of ours.

opportunist
opportunist
9 years ago

Maximum 5 Kids per family osafuna achoke

johnM
johnM
9 years ago
Reply to  opportunist

five children, that’s too many. A family should have not more than three children

Mike
9 years ago

you cant heal Mw

Read previous post:
Zambia’s Cleo Ice Queen to rock Malawi: Gwamba, Lulu to curtain raise

Zambia's rising hip-hop queen, Cleo Ice Queen arrives in the country Thursday, ready for City to City “Summer Returns” Tour....

Close