Email a copy of 'Malawi now has new nutrition policy, says Muluzi: First Lady to launch it' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

1 Comment
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ndele
ndele
5 years ago

koma nde ndi zoonadi malawi wasandukadi play ground. cili cose launch launch launch . zinthuzi timakhala ngati family ina ikutipangila. no 3 kusauka pa dziko lose koma every ocassion koma dzinsalu mbweeeeee, zimaluwa mbweee for what???????????????????? bwanji sitimaziona kwa azayhu mmaiko maka a cizungu omwe ali olemela kuposa ife. kodi mitu yathu ili mmalo.
mmabwera ku misonkhano mutazipolisha koma mukukawaonao ali mbuuu njala usiwa , mitu yanu imagwila. kodi zimasowa kuzimangilila thooo , ma suti dzuwa ili koma mukupita koona osowa. mitu yanu imagwila, pena munazipeza zinthuzi kocaica, mwa ngozi????????????????? eh

Read previous post:
Sports Minister hails Malawi queen of the ring Bashir for Commonwealth title win

The Minister of Labour, Youth, Sports and Manpower Development Francis Kasaila has hailed female boxer Anisha Bashir for winning the...

Close