Email a copy of 'Malawi nurses warned there will be consequences if they photograph victims' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
misozi banda
misozi banda
7 years ago

zandikumbusa ijayo nesi wa pa mwai anaulula za matenda a odwala kuti ali ndi ezi.molini kawalewali
siwasopano amaoneka kuti ndi nurse wakale ndithu.
vutoli likucokera ku school amayenela kuphuzisidwa zose asanaponde pa ward.
amakhala pa nurse station kuwerenga ma file a ma patient ndikumakambilana. patient rights ku malawi kuno nde mdi ZILO tu.

Biti
Biti
7 years ago

Amenewo ndi A Chemwino komanso ma nurse musiya uhule kuyenda ndi azimuna okwatira too much

Chilungamo Chimawawa
Chilungamo Chimawawa
7 years ago

who told you a nurse is always a woman. sukulu njofunika kwabasi. vuto ambiri inu mudathwawila pa dzenela kkkkkkkkk

NAMWINO
NAMWINO
7 years ago

THEY SHOULD NOT HAVE THEIR PHONES WITH THEM WHEN THEY ARE WORKING. IN OTHER COUNTRIES THEY HAVE LOCKERS. IMAGINE SOME OF THE NURSES EXPECIALLY MAKE NURSES THEY NUDE PICTURES OF WOMEN.

chanco
chanco
7 years ago

ngat a tutor anu ali anurse muwafunse kut nanga akazi anu azigwira ntchito yanji? teleku man ao ndi a nurse?

amuna
amuna
7 years ago

ada awonso ndi a nurse kkk sali serious ndi moyo wao,,, nde akazi azitan?

Nurse
Nurse
7 years ago
Reply to  amuna

Mbuli check definition of nurse

amuna
amuna
7 years ago

vuto amakhala atopa ndi kusuka mabala, nanga amunaonso ndi ma nurse,,, ? by difinition of nurse a! ine manyazi kumuza munthu my position kkkk

Read previous post:
Speaker casts rare tie-breaking vote, irks government side as Malawi opposition brings electoral reforms motion

Speaker of Parliament, Richard Msowoya, credited for taking a neutral stand in running Parliament’s affairs despite being vice president of...

Close