Email a copy of 'Malawi opposition criticises anti-corruption chief appointment: MCP calls it ‘cosmetic’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

58 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Manzy j
9 years ago

Koma kabwila yu atangomupatsa dzikoli kuti alamulile kwachaka chimodzi angachite chani ameneyu? Kutsogoleratu anthu sikophweka akabwira. Mumafuna azikusankhani inu kuti mukhale maminister kapena mukufuna atakusankhani inu kukhala ku ACB? Osamaonetsa mkwiyo wanu woluza zisankho pomangatsutsa chilichonse musaganize kuti muzapeza mavoti pomangoti kukamwambe pachirichonse. Kodi kondowe ndi mulomwe? Akabwila kodi ndinu anzeru kwambiri mmalawi muno? Muzizipatsa ulemu pliz. Kabwira amafunisitsa akulamulira komano ndizosatheka. Tamango pangati chitukuko kwanuko osamachedwa ndikuchita pholoso. Nthawi ya kampeni inatha.vomelezani kuti APM ndi president wa malawi. Chomwe ndikudziwa ineyo ndichakuti kabwilayu amadana ndi ma president kuyambora Bingu, JB and APM onsewa kwaiye palibe chomwe achita. Olo inakakhala… Read more »

Mulira Sitinati
Mulira Sitinati
9 years ago

Kodi wabwino atani?adzasankhe bambo anu?mesa kodi enanu akakusankhani mumakana?musatitopese munangomva kuti opposition ndiye kumangongosusa zili zonse?respect urself munthu saipa zonse,timakipatsani ulemu!mukumbuke kuti nthawi yopasula inapita ino njomanga.pple wil judge u by ur words!

nzeru zayekha.
nzeru zayekha.
9 years ago

Musiyeni APM agwire ntchito yomwe akudziwa kt ingathandidze dziko but mukamakokanakokana muzingobwezeresa zinthu mbuyo. God bless my country!!!!!!!!!!!

Wawa Phumisa
9 years ago

So it is only MCP and PP doing the checks and balances. UDF inatafunidwa hahahaha. Bakili is a sold out. UDF is his asset. Some of the smallest parties combined cannot even make sense to all Malawians. By the way, Jumbe and Davis Katsonga what were they doing at state house? I thought these misguided gullible politicians deregistered their briefcase parties?

Tengupenya
Tengupenya
9 years ago

birds of a feather cannot pluck each others’ feathers.

Tengupenya
Tengupenya
9 years ago

financial experts to prosecute financial thiefs!

akatswiri
akatswiri
9 years ago

The Job the deputy Acb, will be tough since the Director is layman in Law,what a wast.

ken
ken
9 years ago

Just shut up woman. Who do you think you are? Munthu omangochita critisize zilizonse basi. Ndiye muliratu simunati. DPP Woyeee Bravo APM

Hardwick Kametah
9 years ago

The appointment has bn made just to hide wh@ the dpp gvd stole during the Bingu time,im feeling sorry for my fellow poor malawians,nothing tangible has hapened sor far bt only dismisals & new appontments(which also favours mlakho)kkkkk

Uchitsiru Sasekana
9 years ago

Why couldn’t the government let Mr Rezine Mzikamanda finish the job he started first and then replace him after he had successfully delivered what he was required to achieve in this case we are looking at a very complex issue cashgate whose main culprits are Top government officials, should we therefore conclude that the President has something to hide by this sudden and awkward appointment of a new ACB Boss ? I have noted with great concern that each and everytime a new government is ushered there is always pressure and confusion when it comes to controlling officers in very… Read more »

Read previous post:
Chakwera, JB, Nyondo snub Mutharika’s luncheon

Leader of Opposition and Malawi Congress Party (MCP) president Rev Dr Lazarus Chakwera on Thursday was no show at hilltop...

Close