Email a copy of 'Malawi Parliament meets on K572 billion cashgate' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

20 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Nebraska
8 years ago

Komatu you Parliament will make the lady mandasi seller aka- former president- not to come back. In her reign, MK350b out of the MK577b went missing. Mufuna azimangilire? Tamufunsani Nzomera Ngwira akuuzani kuti izi ndizoona.

Binton wakale
8 years ago

Akufuna allowance paja fodya malonda sanayende bwino kukokera.Mukudziwa ndalama tilibe zikuvuta basi mutinamize kuti mukambirane za 572 billion yet you know khoswe ali pa mphika.Chabwino pitani koma akufuna kwabwino no allowance sankhani amene ali kufupi aziyendera boma lilibe ndalama zomwaza.Ndipo inuyo ndinu maso athu ndipo pansi pamutima mumamva kuti ndalama zikusokonera mdzikomuno basi munali phee kudikila allowance iyiyi?Munyumbamo mukapezana mumakumbukira kuzikwesera malipiro anu kaye cash-gate later on eti? Ndiye lero anthu wambawa akoma poti inunso pali soup?Anthu womvetsa chisoni you take us for granted one day you politicians believe me you shall dance to our tune. Ask yourself where is… Read more »

chidongo John
8 years ago

Malawi parliamentary mwangosawa chochita if one of you knows the deal then go open the case against whose Peter or Bingu and prove that he is stole K572 billion and K92 million respectively, beyond reasonable doubt. None is above the law. Osamangosokosa ngati court kapena police simudziwako. Ngati simutero ndiye muzingokuwa ngati galu amene amangokuwa chikuwekuwe. Kakumaneni Ku khoto. Kaya mulipo kagulu pitani. Kaperekeni umboni. Ngati mukupangira za cash gates. Munthu sangamangidwe ngati simunakamudulire chisamo or mutamuona kuti akuba. A mene akudziwa amumangitse.

WOYEEEE
WOYEEEE
8 years ago

Kikkkkkkkkk #1 you are supa boy,was it not like this time we wanted to impeach his bro,M’bingo wantalika?

Chonena sowe
Chonena sowe
8 years ago

Agwileni a DPP aonjeza kuba. Onse muwakokolore a Lowe. Aululana momwe akudyera.

bottomani
bottomani
8 years ago

Sub-human primates.

Mamwene
Mamwene
8 years ago

Bt y o dis iz happenng in dis very poorest cost, do dis ppo don’t hv pity with others’ relatives who lack madicine n basic needs mmmm shame on them!

Thom Chunga
8 years ago

Why is that K1.7 billion cashgater left scotfree? He should be arrested as JUSTICE SEES NO FACE.

Genuine Patriot
8 years ago

Hating Peter won’t help. We know its JB who ruined this country with her Cashgate.Mfiti. Tell her to come come back. What is she running away from. The arrest warrant is patiently waiting for her. Coward!

hisbolla
hisbolla
8 years ago

Where did u c MLOMWE wanzeru? Kkkkkkkkk

Read previous post:
Airtel to fire up Malawi Lake of Stars festival with lots of freebees

The 2015 Lake of Stars fiesta is finally here to rock and roll fun lovers in Mangochi this weekend. With...

Close