Email a copy of 'Malawi peaceful protests today: What you need to know' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
lusiano banda
5 years ago

amalawi azanga tikuvutikinji mulungu anatipatsa mnyamata amene alindi masomphenya amarifunila dziko lamalawi koma ndi anthu ake zabwino sakhala ndimbali or atampatsa ndalama zochuluka bwanji koma iyeyo anama pachilunga saopa koma amanena zokoza Malawi ndizothekatu amalawi tose kunena chimene chikufunika kuti dziko liyende bwino posankha fundo zabwino osati kumasekerela atsoreli akuba omwe akuvutitsa athu ambiri chifukwa akuika ndalama zoyendetsela boma mmatumba mwawoo ine ndimasapota sir lusius banda ndi kusabisa may kwa amalawi ose ndipo amalawi nose munakakhala ngati ine tikanangoti change nthawi imodzi paribe angatsutse gulu akadachokapo okha

peter georgce
peter georgce
5 years ago

Malamulo akulora ziwonetsero Peter Mutharika , Goodall ,Kondwani Nakhumwa ndi akatangale kwambiri aDPP agulukunyinda awo apanga zawo motsogozedwa ndi ng’ona zawo.

dinky
dinky
5 years ago

ndiye dzulo munali yaviyavi inu a diphiphi zazii basi abakha inu mumatikwana kwambiri

dinky
dinky
5 years ago

tikuti ma demo omwewo basi ndiufulu wawo

#DzukaniAmalawi
#DzukaniAmalawi
5 years ago

Why would DPP allow Public Order Police unleash unnecessary force on its own people. Why would DPP mobilize its unruly members to cause hard to its own people. Why would DPP not listen to its own people when they’re expressing their anger. DPP should learn to engage with the very people it is governing to be a better party.

Paul
Paul
5 years ago

The organizers need to share us their tweeter handles and whatsapp number – keep us on the loop

joseph.zibophe
joseph.zibophe
5 years ago

ma demo omwewo basi asamajaire

Paul
Paul
5 years ago

The organizers need to share us their tweeter handles and whatsapp so that are were kept in the loop

Paul
Paul
5 years ago

The organizers need to share us their tweeter handles, and whatsapp to keep us the loop

Read previous post:
Malawi woman believed dead is found alive 3 years later: Eunice Monjeza

The Monjeza family of Katoto residential area in the city of Mzuzu had a thanks-giving mass on Saturday  April 21...

Close