Email a copy of 'Malawi players Chawanangwa, Banda sign for Mozambican clubs' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi players Chawanangwa, Banda sign for Mozambican clubs' to a friend
Digital Satellite Television DSTV customers in the country now have a wider choice for subscribing to service providers as a...
Bullets would have managed to buy those players from Silver by cash not by lan
Some BB fans are still wallowing in past glory. This is 2015 not 2004 when you had the financial muscle to acquire any player of your choice on the local scene. No wonder you assembled a strong squad that was ready to compete with the best on the continent. Pano mudasauka kwambiri kotero kuti ndalama zogulira osewera pachilungamo mulibe. Ukatswiri umene muli nawo pano nkunamiza osewera kuti akubwera ku timu kwanuko awonjezera mwayi wokasewera kunja! Ndi kale lija! Vomelezani mmene muliri pano!
Is it Costa de Sol or HCB de Songo?Please clarify.Welcome to Moçambola and all the best and success guys.
Better than umphawi wa ku BB.
Congrats silver strikers, palibe team yakuno ikadatha kugula pamtengo umenewo bwenzi mukungokangana ndi ngongole basi. Even Chawa himself testifies kuti uko kulibwino than kuno, all the best Chawa and Frank
Mwapindulanji a silver strikers pogulitsa puleya K3m pongofuna kuthawitsa ma players kuno ku malawi kumene mukanalindira kawiri ndalama ngati yomweyo? Nsanje siipindula, lero mwakulitsa udani ndi matimu a kwanu kuno…..Muli ndi tsoka lalikulu ndipo mumva m’bebe ligi ikayamba….. Mpaka timu yanuyp ithaaaa!
Osagulitsa aja agulitsidwa pa mtengo wamakaka!! Shame!!
Zilibwinobe anyamata akaone kusintha awa.Next time ndiwaku john basi.O de best!!!!
Gd news
koma silver matama onse aja mwathera pamenepa pa three million