Email a copy of 'Malawi players Kawonga, Kachimanga in Mozambique for trials' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
bobo
bobo
9 years ago

we dont to sell chawanangwa to bullets remember chimango kaira saga,zotipusitsa ife a silver strikers

zion
9 years ago

Ma player a Bullets amachita kusowa ngakhare sopo wochapira mapanti ndi socks. Masapota awo ndi ma official ntchito kuba ndalama za mmagate.

Katswiri left wing'a
Katswiri left wing'a
9 years ago

Congrats Silver strikers, mwaonetsa ukholo wabwino. Sitimangolora kuti mwana akwatile paliponse mwachisawawa. Bullets yanyanya kutuwitsa ma players. Kungoluza tima game tiwiri basi kufuna kuwapha ma players.ku Mozambique Chawanangwa will prosper

Petros
Petros
9 years ago

Zaipa lero mwayiwala za chimango.zoona chawa achoke mu basin akagwere mu lichero bullets?

Wa Maule weni weni
Wa Maule weni weni
9 years ago

Chimango Kayira sakukwanira Hahahahaha itanitsani Gaba!

Limbani hammy mtanga
Limbani hammy mtanga
9 years ago

Kupita ku Bullets ndiye kuti chani? Kufuna kuti akatuweko kumeneko? Kukhala ndi masapota ambiri kumatanthauza kusamala munthu kodi? Bola ku mozambique akagulako ka LIFO,prayer kumakwera kabaza zoona?

mwadzaangati
9 years ago

Silver has done good to let chawa and kachimanga go to Mozambique nt as it was to let them go to Bullets hope alesson learnt do good to others so that they do good to you or be nice to pipo on your way up cause you will meet them on your way down kkkkkkkkkkkk nkhonya yobwezela kuwawa

Yankees
Yankees
9 years ago

Mumakafuna mkazi omukwatila mulibe kodi nyumba yogona? I told u to go abroad zikanayenda kale kale, dalirani aFisher, Sailes, Kabichi akakatchoka tidzakubwelekani ma Prayer but not now. Pajatu nafenso atipatsa kathumbatu!!!! Kkkkkkk.

nchiani kodi amalawi
9 years ago

maclub apamalawi.kukhala ndikukhala maplayer kumaagulitsa kumozambique??

Gona n'kuphe sali patali
Gona n'kuphe sali patali
9 years ago

Kawonga won’t play 4 bullets or zitachita kuvua bwanji. Bankers will neva 4get chimngo kayira’s saga!

Read previous post:
NACgate and challenges of objectivity journalism in Malawi

“Many journalists now are no more than channelers and echoers of what George Orwell called the ‘official truth’. They simply...

Close