Email a copy of 'Malawi Police arbitrarily shot and kill two in Lilongwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police arbitrarily shot and kill two in Lilongwe' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) president Dr Lazarus Chakwera on Sunday welcomed political prodigal members back in MCP fold at a rally which...
In countries like South Africa a shoot to kill is implemented when criminals have fire arm pointed at police officer, but in countries like Malawi, shoot to kill is for what?
Koma akapha wapolice ndiye mumakondwa
We are living in fear because of thieves and armed robbers. If what people are saying is true, then we should not politicise issues here.l Policemen are at work
chonde asiyeni apolisi agwire ntchito yothana ndi mbava, luka ndi kawongayo zinali mbavazoospya musanyoze apolisi musalowese ndale pa nkhani zambava, tafusani pa vinthukutu zambava zimenezi kuchilumba
Ngati uli mbava sulimba ngongole yokatenga usiku yamtundu wanji and moreover mukudusanso kumandanso mbava ndi zomwezo it’s not a mistaken identify.
Ken msonda ngati nawenso uli mbava tasala pang’ono kukushuta wamva?
MHRC,also document the killings of Police Officers & Innocent Civilians by these SAME CRUEL ROBERS.
Iwe Ken Msonda shut up
Ndikuyamika ntchito yabwino yomwe a Police mukugwira yokupha anthu osakonedza dziko. Komanso musamanyang musamayang’ane nkhope ayi chifukwa enawo ndi abale anunso.A cash gatenso aphedwe mosayang’anira nkhope
Inu anthu musavutike an amenewa ndi mbava zoopsa ask anybody wa ku chilumba akuuzani za ana amenewa achi Kawonga mbava wina amwabera uncle ake a mwenelupembe Kawonga mbava yoopsa.tapitani ku Chilumba pafupi ndi galison mukafunse za ana amenewa.Peolpe are rejoicing …kaya winayo watsitsimukiranji ….ma nurse ndi ma doctors tachitani naye ameneyo