Email a copy of 'Malawi Police arrest 17 boys in local 'Boko Haram' gang' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police arrest 17 boys in local 'Boko Haram' gang' to a friend
The Public Service Reforms which is being initiated by the Malawi government are being frustrated by the people who are...
Comments are closed
14yr old acting as boko haram? Anena zambiri ana amenewo. The real boko Haram is coming
Asapite ku ndende but keep a very close eye on them.If they do it again then they deserve prison life. Nanga kuba phala tinganene kuti ndi mulandu woti mpaka ukanenedwe mukhoti? The issue here is not serious,they just need proffessional counselling. Dismantle this bad company rather.
This article is truly written by a foolish insensitive unprofessional writer. I say writer because to call them a journalist would be insulting to those who are journalists.
Boko haram is not a catchy term to be thrown around in titles to get views. Implying that boko haram are in Malawi is unprofessional, irresponsible, insensitive to real victims of boko haram and inciting unnecessary fear.
Send them to mpemba boys home
Apo ayi alembeni ntchito ku utsilikaliko !!
writing on the wall
ndchan cheni cheni cikucitika dziko lapansi dis thngs its seens lyk dis is a past days bt kungoikiza mapemphelo dziko lathu lamalawi kt zimenezi zithe bas
ma gang ‘wo si Boko Haram,ndi Boma Haram
Vuto simakolo awo Ayi.Mwana amatha kuyamba zoterezi chifukwa cha azimnzake ocheza nawo.Monga mmene mwamvela nkhaniyi Panali ana ena a mchititidwe umenewu ndikale omwe amakakamiza amnzawo kuti awatsatile ku gulu lawoli.Koma ngati sakhala membala wagululi amapangidwa nkhanza chifukwa simembala wawo.Musawapake makolo awo apa.Kholo likhoza kukhala losamwa mowa pamene mwana wake amamwa.Chambachonso chimodzimodzi kholo osachidziwa Chambacho mwana mkuchisuta.
vuto sianawo koma makolo awo.mwana wazaka 14 akavute kumpanga handle.