Email a copy of 'Malawi Police arrest father, son for whacking suspected thief' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police arrest father, son for whacking suspected thief' to a friend
Malawi Police Service (MPS) has placed K1.5 million ($3 333) reward for information leading to the arrest of theĀ assailants...
Yap
mtumbuka ameyu eti?
So police don’t like competition in killing thieves ?
But u police guys you shoot to kill suspects
Does the police consider that these thieves come well armed? How can you take a well armed life threatening thief to the police unless you physically subdue him/her? Palibepo nkhani apa.
Mmm nanu apolice musamakhale busy kusaka yemwe wachotsa ma limbs kapena kupha mbava.Zikatere mudzisangalara coze u never know kut mawa akanakaba kwandan?,mwina nkunyumba kwanu kapena kwa m,bale wanu!.Zimatikhudzatu tikamamva kut wapolice waphedwa ndi mbava.Timalakalaka titakhala IG/ president nthawi yomweyo nkupha mbamva zonse including za cashgate ngangale ndiizo zomwe zayamba kupha anthu…so bad.
Aniyake zimbeo chonde atulutseni,sanalakwe!!!!.
Kill kill kill
Kuba ndi kuba basi . Bolanso ya maligaments nanga shoot to kill
Kupha mbava sikulakwa chifukwa ndigawo loteteza munda wake munthu omwe amadalira moyo wa tsiku ndi tsiku. Enanu akazaba kwanu muzaona kamwini sikachepa
Sanalakwitse iyeyo nzimbeyo inali yake panyopake,amuchepetsanso akanangochipha ngakhalenso kuchiotcha ngati mang’ina,nanu apolice mukusowa ntchito eti,munthuyo anakhetsera thukuta lake,iye manja lende,chizeteeee