Email a copy of 'Malawi police arrest man for scorching step son for wrongs of mum' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi police arrest man for scorching step son for wrongs of mum' to a friend
Police in Malawi have revealed that Pelekani Malunga one of the arrested suspects in the K100 million bank robbery is...
Minyama ikafuna kukutsata you never know
Alcohol is not adefence he had an intention already and is deserving stiff punishment for others yo take a lesson.
ONCE balaka alwayz balaka kumudzi kwathu ndimakunyadira tiyeni tonse anthu akubalaka tizunguze 2015 kuposa apa
Tatopa ndikumva nyasi za kubalaka.
Inu kodi kumeneku si kwawo kwa soldier woimba uja? Nanga bwanji osapanga za u soldierwo kumeneko ndi anthu akuvuta ndi za usaveji zo.
Kodi Asilamu mwayamba kumwa nao mowa wathu uja eti?? Mwaona vuto lomwa mobisika?
kachasuyo anali wongolengela Zomba basi ,mission inali ya mfana yemweyo,asaname.
Ndiye balaka imeneyo
Zilibwino kuti wamangidwa. Ngati ndi mowa achimina.These kind of pple tarnish the image of our nation. Zaka 32 kumaganiza mopepera ngati khanda?
Balaka!!!! Kwao kwa Getrude uyeni.