Email a copy of 'Malawi police arrest Rev Munthali of MCP for obstructing First Lady convoy' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi police arrest Rev Munthali of MCP for obstructing First Lady convoy' to a friend
The UN in Malawi is concerned about several recent incidents taking place at the beginning of the electoral period and...
Why couldnt the security guys shoot the unknown vehicle? This is carelessness of highest order from the part of First Lady’s security detail…..
Moris Munthali ndi wa chamba. Ignorance has no defence. amafuna atchuke kuti achititse ngozi first lady. anthu ngati Moris Munthali oterewa ndi amenenso adachititsa ngozi Pricess Diana mpakana kumwalira. Nayenso munthali afuna kuchititsa chimodzi modzi kuno? Mumfufuze bwino ameneyu, akudziwa chimene amachita. kulimba mtima kotani kumeneku kokathamangitsa mkazi wa pulezidenti panseu. azitibulidwa makofi , isn’t it attempted murder but failed? Kodi ma body gurd akanapanda kuteteza pomubloka chikanachitika ndi chani. Ku satanic kwanuko mwabwererako chabe mwalephera kukhetsa mwazi
Abusa kusaka kutchuka kumeneko? Muziti DPP yakumangani mukumenyela ufulu anthu? Kkkkkk kodi MCP yazaza ndi azibusa oganiza mosekesa bwanji???
Palibe nkhani yomangila munthu wamulungu apa osangomanga miseu yayikulu bwanj these are public roads not presidential roads…iwowo nde azingophangila chilichose umbuli basi
Where are the helicopters that Kamuzu,Muluzi and Bingu used to use. Pitala and his wife have been disturbing us a s motorists for some time now. Does it mean we are poorer than the Kamuzu Days. This is because dpp is busy stealing like Jeff wa Jeff says in her conversation with another thief Nankhumwa. What is cheaper to have a convoy of 21 vehicles and policemen lining up all the 320 km. We are a shithole country or we have a shithole leader.
Kenaka akayamba kua user muziti akuononga chuma cha boma.
a winston msowoya ndinu wombwambwana
Only an idiot would believe this story.
komanso muwamange ma dpp cadet who blocked kaliati’s vehicle. zausiru basi. getrude mutivute naye timadya kwawo
Ndinnkazi wa pulezidentitu
I thought this guys are trained to cruise at supersonic speeds! how come an ordinary driver can manage to cruise at the same speed?kkkkkkkkkkkkk
President wakalamba azipita …hiyaah!!!!!!