Email a copy of 'Malawi police calls for speedy trial on Neno killings, condemns act' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi police calls for speedy trial on Neno killings, condemns act' to a friend
After queuing on an empty stomach to buy maize at Ndirande-Chinseu Admarc, one woman fainted as buyers fought for the...
Calling Judgement Basi from above dziko lakanika ili! mwana chasowa mpakapano koma zalero changu!
Kodi munthu uja mudamtola padenga ku Ndirande-Makata ali buno bwamuse mulichelo uja, Ndindani? Thindwa asamakupusiseni akudyera mmomo. Mzungu amene adalemba witchcraft law mukunenayi kwawoko ufiti ulipo. Hence: the words “witchcraft”. “wizard”. Inu a police ndinu amene mungaliuze boma zoona chifukwa ndinu amene mukukhala ndi anthu kumidzi ndipo nkhani izi mumazitsatila bwino. Fufuzani posatengera NGO kapena President. Get to the root. Umanena chatsitsa dzaye. You are the professionals. Ndipo timakudalirani.
The range of suspects age raises a lot of questions. Since you have already stated that the Malawi laws do not recognize witchcraft’s existence, do you think any complainant against witchcraft has a chance to be heard in a court of law? I think this is high time to review this law and call a spade by its name. The bible recognizes witchcraft. Why is our law so defensive. I just think that its this defensiveness that is causing the rise of this lawlessness. Can somebody over their look into this critically.
So its possible for Malawi police to nvestigate a murder fast? Excellent news MAlawi Police Service! Please do the same with Chasowa’s and Njaujus murders! EEEhe bwanji pamenepo? Mupanganso fast???
Fast ndi zaeni.
Koma zanu “still investigating”
ZA ISSA NJAUNJU ZIRI PATI?