Email a copy of 'Malawi Police, vendors clash: First Lady school torched in Lilongwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police, vendors clash: First Lady school torched in Lilongwe' to a friend
Students of the University of Malawi (Unima) have given authorities up to November 1 as a deadline to reverse a...
Anthuni tiyeni timvere boma lathu. wolemba nkhaniyi akuti mavendors apite ku official flea markets, kusonyeza kuti kopita iwo kulipo kale. Tsono chochitira nkhondo ndi mapolisi ndichiyani? Apolisi, mangani anthu osamvera lamulo.
Komanso pikitchala iyi yaulula kathu kena kamene ambiri sanali kudziwa za Lilongwe.Bwanji City Council ipeze Investor womanga nyumba za maofesi ndi zongona zija zazitali kupta mulengalenga (10 or 20 storeys).Tikatero City yathuyi idzakhala ya kumatso kwa anthu.
koma mavenda akanamvetsa coz anapereka notice a city kuti aliyense achoke m miseu nanga chimene amakakamilamo ndi chani? Chisakomele mbuzi kugunda galu.
koma kumeneko
Ine chisoni, chabe ndi anthu ozuzika ndi zosayenera kuzuzika nazo, kundiwawa Moyo ndi anthu amene akusangala ndi zosayenera, kusangalala nazo, choncho dziko ndi la zonse tionetsetse zoyenera kupanga
Provide them a legalised place then…
Achita bwino amazolowera
umbava uchepa bwanji anthu opanda nzeru, tsono mwawathamangitsawo akadya kuti? ngati simunabeledwe muziona tsopano tonse tiyamba kukuberani olemelanu dikirani
penapake a Malawi lets learn to love our country, we are not the only poorest nation in the world. Palibe nkhani yolemba kuti Malawi is one of the poorest nation apa, atolankhani ena kumvetsa chisoni bwanji? kodi kusauka ikhale nyimbo basi everytime you write about Malawi basi pamapeto pake “poorest country” enafe sizimatiwaza olo pang’ono mwanva.? Who doesn’t know that we have a lot of poor countries in Africa?
and at picture is taken in heart of Lilongwe, oh no after 50 years of independence and our capital city looks like a trading centre in dowa, look at the poor road, dust and ugly one story buildings, does Lilongwe have a city council and mayor, roads authority, town planners, school has not helped you a bit, you are all a disgrace to the country
mwalakwa kuwathangitsa anthu omwe amayala malonda,iwo samabera anthu,kwao nkugulitsa malondangati ndi ukhondo nkwabwino kuthana ndi masueji omwe amaphulika tsiku ndi tsiku nkati mwa tauni,amalawi anzanga tiyeni tosiye nkhaza izi ndi nkhaza!!!!