Email a copy of 'Malawi President Mutharika 'falling' picture goes viral on social media' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi President Mutharika 'falling' picture goes viral on social media' to a friend
United Democratic Front (UDF) has sternly warned the party's vice president Iqbal Omar that he risks unspecified action if he...
nayeso ndimunthu ngati ife tomwe
Kasala komaliza kkkkkk
Ndikumva chisoni pa zolemba zanu .akanagwa wina sizikanalembedwa po mumamtenga president wina aliyense ngati chitsulo chisachita dzimbiri nthawi zina tiyeni khale oganiza bwino tisanapange zinthu..
THINGS FALL APART, THE CENTRE CANNOT HOLD. A QUOTE FROM CHINUA ACHEBA. WE CAN NOW SEE WHAT IS HAPPENING IN OUR OWN LAND
zimachittka zukani madala madala
Nanunsotu a nyasatimes pena pake mukuyenjeza, ngati anagwa Yesu mwana wa Mulungu kuli bwanji ife anthu wamba.Ndiye kuti mukanakhalapo nthawi ya Yesu mukanamalembanso zimenezi. Zitiwonongera mbiri ya dziko mukupangazi. This is being irresponsible, why exaggerate things?
Muthalika kufanana ndi Nowa klkkkkkkkk
Anganga 193, it’s Leadership.
za ziiiii!! inu simmagwa???? chifukwa ndi presdent nde basi!! musokosele!!! i stll lov u mr muthalika & gate well soon,,,,,, nganganga pambuyo panuuuuuu!!
Moya mwakula basi, ntchito mwagwirapo.