Email a copy of 'Malawi redeploys diplomats: Bowler, Mhura, Sawerengera on the move' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi redeploys diplomats: Bowler, Mhura, Sawerengera on the move' to a friend
Angry villagers on Monday morning stormed a police unit in Dedza, took out a suspected murderer and killed him in...
no clear strategy. just something that dumb people would think is a good move
Atumbuka kwanu kunatha. Ntchito kuononga ndalama yathu yamisonkho kuthamangitsa chikopa pa stadium nkumaluzanso mipira yonse. Atumbuka United..shaa! Msowoya, Mhone, N’gambi, Mhango, Mkandawire, Chirwa, Pagolo Munthali, coach Mtawali…what else do you want?
Welcome to New York Mr Mhura
MALAWI IS A FAILED STATE… A FOREST FULL OF JEALOUS UNEDUCATED BABOONS!..
One thing Mhura should desist is to continue writing grafitti on embassy walls. Old habits die hard.
As kodi muuti nji Mesa dzana mmati azibwera? Lero mungowasintha mozungulila? As kodi Maggie mblizi ndi oimilila can I Ku Washington? NDE nayeso amapanga za mmaofesi a boma kusintha anthu? CE sawerengera koma munamuuza Maggie yo? Kkkkkk
Koma NDE dhillo azimai.
Tsopano nduona kutha kwa Malawi zikafika poteolpo
Nangodusamo
Malawi is a failed state. Ntchito zopatsana, even to the poi9nt of kusankha. I am not complaining.
Education does not remove ones stupidity proof chapondix.
It is blatantly obvious that lomwes are being favoured at the expense of chewas, tumbukas, ngonis etc. chapondix, I thought you have a phd is it in tribonepoticity?. the dpp honeymoon will not last forever, mudzapweteketesa abale anu ndithu
Ma recalls akuchedwatu, onse okhalitsa more than 5 years adzipita please to give chances to others. Ku Ethiopia and egyot offices taunikakoni.
Mwana wa kaliyati ndi mwayi dausi still in London. Koma mukuti reducing. What they are doing there….. Search me!!!!