Email a copy of 'Malawi to increase salaries of junior civil servants from December: 2015/16 National Budget' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi to increase salaries of junior civil servants from December: 2015/16 National Budget' to a friend
Football Association of Malawi (FAM) President Walter Nyamilandu has lived up to his word not to stand for a fourth...
ya
Anthu amenewa akutiyenda Njuga kwambiri Googall akadafotokoza kuti ma Juniors ndi awawa komanso ma Percent mwakuti koma ngati kagulu kena sikawonjezeredwa ndalama ntchito ivuta komanso december ndi kutali kwambiri Budget mwapanga pano increament December,Munatani ka Budget kanuko osapanga mu December mo? We r watching you.
who are junior staff? In my understanding all those who do not have any kind of privilege such as professors senor Lecturer since their salary is a clean wage. Mind you the issue is about public servant not civil service only. There is need to clearly define who are Juniors in public service.
stupid gvt
Vinyophilo vanu agalu inu osangokhala chete bwanji u think December is tomorrow? How can you tell a hungry person that food will be served in two days time?
thus talking
i thnk these greedy creaturez em dnt care bout us,ppl hu voted,ds z pc ov shit
Tsopano majunior staff wa muwachita exempt misonkho mukukwezayi kufikira dec pamene mudzawakwezere salary? Ngati mudziwadula misonkho mukukwezayi pa salary yao yochepa kaleyi, will it be fair? Anthu amenewa pofika dec adzakhala amphawi otheratu moti ka % mudzikeko kadzakhala kopanda tanthauzo! Where is ma trade union? Cso? Paja nonse ndi ma senior servants, zanu zinayera eti?
CSTU mungokhala chete pamenepa? Lets stage strikes otherwise izizi sizoona
Mukuti new salary in December is it fair? Pomwe inu ma MP mukangoti K20,000 per day sitting allowance nthawi yomweyo khethekhethe koma poti ndi Junior staff mukuti after seven months. Adanenatu paja Sikusinja kuti nkulakwatu uku anzanu satero chidani! Mukutinso mwathetsa students allowance for public Universities kodi a bomawa apangapo chiyani kuti ana athuwu aphunzire ku University. Think about poor parents in the rural community whose per capita is very low and they even failed to pay school fees for their children at Community Day Sec. Do you think those people can afford to pay K275,000/semester at the university. Mulungu… Read more »
Gondwe kumaganizako ako anzako. Chaka ndi july otsati za dec zakozo. Aphungu chonde help us plz musalole za fodyazi chonde. Mcp ndi pp tili pambuyo panu chondee