Email a copy of 'Malawi trainee teachers go five months without pay' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi trainee teachers go five months without pay' to a friend
In a bid to address communication problems between the deaf who learnt sign language at school and their parents or...
IT IS NOT ONLY THESE, NO, EVEN THE FULL QULIFIED TEACHERS ARE NOT BEING PAID, ALSO THE FIRST TEAM OF 2013/2014 THEY HAVE NOT RECEIVED THEIR SALARIES, WHAT A SHAME IS THIS ———PLEASE PAY THEM SOON, UNION SUPPORT THE TEACHERS.
NATION MSOWOYA — WHAT DO YOU MEAN——- YOU ARE NOT AWARE, JUST BECAUSE YOU ARE ENJOYING YOUSELF,YET OTHERS ARE IN TROUBLES AND FACING PROBLEMS, PLEASE THINK TWICE.
Ali fulishi
Nafe a machinga ttc odl 3 tikufuna ma K60 thousand athu…mutipase mwezi uno usanathe musangokanirana kumeneko…mixiiiiiiex mulemerere pa ife???
Even Those Who Had Already Completed Last Year,awaiting Postings At Bttc Are Not Yet Paid Their 5 Month Pay. Pitala Samala, Anthu Akupemphelera Kuti Upite Mwachangu Ku Mpumulo Wa Bata.
Inu mukudandaula trainee, boma silikulipira aphunzitsi eni eni…ine ndili hubby wanga was deployed from Chanco to a school in Dedza last september yomweyo koma mpaka pano no salary, no what, nothing!!!
double wahala
kumalawi kuno umbava too much ndalama zawo maziphunzitsi zapita kuti? bola ma tranee apolice akumawa bela ma k 11,000 mudzina la accomodation.nde umbava okhaokhawo ichokabwanji pa k 1000 kufika pamene? ka allowance kungokaduladu nde mkumayembekeza kuti umbanda utha,iwalani zhmenezo.ku educaxion konso kwa dzadza mbala zokhazokha.
Not only lttc but also karonga ttc… 4 month without pay…how we are going to survive??
Ndiye akuti kuli anduna ma PS, ma directors kumeneko. Tandiuzeni amachita chiyani must office from 1 to 30?
Y these rabbish things only happen to primary teachers ? Govt officials please b responsible nawonso ndi anthu ngati inu nomwe