Email a copy of 'Malawi VP Chilima commends smallholder farmers at NASFAM indaba' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi VP Chilima commends smallholder farmers at NASFAM indaba' to a friend
The Arab Republic of Egypt on Tuesday donated to Mzuzu Central ophthalmology equipment worth MK60 million as a way of...
Making government get out of dictating price of crops and removing export bans on all agriculture products would be a better way to encourage farmers than that stupid photo-op.
Bola ameneyu osati chitsiru gogowathu uja!
Kodi utsogoleri wakuba umayenda ngati. Mulungu amazima kuwala konse ndi mphamvu za mu ubongo zomwe. zikatero mtsogoleriyo kuganiza kummavuta. and i dont think kuti atsogoleri amenewa amakhulupilira zoti mulungu alipo
Awa ndi a Vp osati zokuba mabedi ku Dowa zija ayi
APM knows this man can take Malawi forward. Am sure deep down his heart, he is scared of him and his inner circle too. APM kuzikundikila ma udindo yet he cannot deliver. Imagine if Mr Chilima was a Minister responsible for civil service. Zibwana zikuchitikazi atapanga sort out. Koma its good the way it is. Anthu tikuona and we know how hard working Mr Chilima is.
kodi APM angasankhe mphwepwa kukhala vs wake?? muyesa ngati ndi bakha uja amangsankha wina aliyese
Shame on u Mr. kungozolowera kunyoza basi. Ambuye akukhululukileni bambo.
Sukunama APM mpatali na pa vice wathuyu. Chapaphewa akuti ankafuna youth kkkkkk
At least something positive from DPP govt. A breath of fresh air. Ndiponso u president WO osangompatsa iyeyu bwanji? Ago go make aka sizikuyendapotu.