Email a copy of 'Malawi woman exhumes albino’s body, arrested' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
shaaaa!
shaaaa!
8 years ago

pajanso ogwira ntchito m’manyumba mwawanthu akuti amapangiranso zizimba kuti mabwana awaonjezeleko ka pa mwezi.akukunamizayo nde ndani.sukulu ndi chinthu chofunikira kwambiri

mphwinthe
mphwinthe
8 years ago

zafika posauzanu.Ndichiyani nanga amalawi?

ARICHO
ARICHO
8 years ago

Aphwache a pitala Muthalika

mbani
8 years ago

Alomwe

Tekninja
Tekninja
8 years ago

Bola ofukula.kusiyana ndikupha wamoyo.osabesa ndalama mpaka kumazikwilira!pali ina ija a president ankakaonelera nyanga za njovu zikuotchedwa.tizafadi osauka mpaka kuotcha cash.

Vincent Villus Vanno Kalulu

Kodi Vuto Mchani Ndiye Mukamanga Anthuwo Wakufayo Azuka?Aleni Mukatero Ndiye Kuti Mwalowelera Ntchito Ya Mulungu.

Benson Chirwa
Benson Chirwa
8 years ago

Shoot to kill ndi deal otherwise they will escape ngati ku Limbe.

Chikuni
8 years ago

What is Kaliati’s comment?

yosefe gambatula
yosefe gambatula
8 years ago

Alomwe kukonda chuma chaufiti.Ndiye Pano afukula manda onse ama albino.Mtundu wakuba,mtundu wokonda ufiti,mtundu wokonda kutafuna gondolosi ndikumagwilira tiana ngati gwaladi.

Keen Observer
8 years ago

Firstly “One Love” what solutions are there that police should do tell them, when Armed robbers are killing our own law enforcers. What rights are you talking about? Have you ever lost a loved thru’ crime????? I guess NO? What rights can give you the power to shoot & kill a police officer whose sole mandate is to protect lives & properties of the citizens. Secondly umbuli mu dziko lathu plus umphawi that’s why 21st Century ino people still believe that Albino can bring good luck. We are really in quagmire.

Read previous post:
Malawi Queens gets MK10 million boost from Airtel

Malawi leading mobile operator Airtel has donated a whooping of K10 million to Malawi Queens as they prepare for the...

Close