Email a copy of 'Malawi women cops face abuses in homes, work places' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi women cops face abuses in homes, work places' to a friend
Government has approved loans for ward councillors who are now entitled to K1 million each. Spokesperson for the ministry of...
Kuyelekedwa akazinu.Mamuna akayende kunja,nsanje thoo. Achite iwe wekha mtudzu mbwee. Mamunayo atanino? Rubbish
Osanama azimayiwa ndiokwiyadi mwina zimayambira ku training school kwawo ndiye ndi mtima okulawo amayamba kuchitilanso mwano azimuna awo. Munthu sungangoyamba kuzunza mkazi wako opanda chifukwa kapena wachambatu nanga munthu wabwino bwino. Palinso azimayi ena apolisi kukonda kuledzera ulowe pub iyi ali mommo upite iyo alikonko ndiye choncho zinthu zingakhale bwino. Komanso nkhaniyi si kupolisi kokha.
strawberyy juice,
Mai yo ndi wanzeru, adaona kut vuto udali iweyo komanso nkutheka kuti amakudziwa bwino lomwe kuti mwina khalidwe lako ndo lonyasa losalemekeza mamuna wakoyo. Mwinanso umakana kukuchinda kumachita ukudziwa kuti ndi mwamuna wako ndipo chakecho udalimbirira pa maso pa Mulungu wako kut ndi chawekhawekha basi. Tsono ngati umankana umati iye asakumenye, iye samafuna kukachinda ma hule a ku Bar ununkha fungo la kondomu akangovula, amafuna Iewyo mkazi wake monga mwa lonjezo lako loti ndi chawekha basi
Prince mpasakuphe,
I totally agree with you guy or girl. The police women are generally very rude. The always and everywhere want to be felt highly and knowledgeable. The have no respect with others as such they can and will not respect their husbands or family members. Police women are very cruel and inconsiderate to the general public. I have no grudges with them but simply saying the truth and reality. Too much mtudzu ndi mwano amayi apolisi even akazi a police (housewives) ndi chimodzimodzi khalidwe lawo. Akhala pagulu amafula akhale oyambirira pa chilichonse.
mkazi wa polisi ndi wapolisi basi si banja ayi
It is common knowledge that marriages in africa are founded largely on the basis of culture. Our cultural values and even the bible explictly stated that akazi inu mverani amuna anu. The challenge comes when the woman want to do policing in the house. In other words most of them fail to undress the police uniform when in homes. I personally dont think it is a question of rights but rather discipline
Candidly I have no grudge against Police women,but of course,generally,they behave impudently and irrespectifully in their places of work it is unusual to find a dignified and well mannered Police woman in Police Stations or offices.They have adopted very outlandish way of life that is beyond our culture,they look down upon their husbands especially those husbands with low income brackets.This habit seems it is worldwide,in Canada,women are .more powerful than their husbands and this many times has ended up in grave sequel.My advise is calm down and solve the dispute amicably otherwise you will end up into more troubles.In Malawi,this… Read more »
Iwe strawberry juice..tanena banja lakolo liri pati pano? Linatha monga? A polisi si a nkhoswe a mabanja. They r trained to decide when to intervene or not to. Atakufunsani mafunso awiri atatu anafziwa kuti mukufuna kukhalabe ndi amunanu. Now i know kuti u r failing to resist the urge of lying to us that u divorced…just saying
Ndani wamisalayo angakwatire mkazi wa POLICE? Mahule? Angakhale ndi banja la ulemu amanewa ? Kukula mtima, Akuti kudziwa malamulo, 4Ja basi.
Malawians let us change our mindset and start respecting our lady cops. Most of people abuse female officer just to test me. Bad manners