Email a copy of 'Malawian Airlines to fly to Tete, Nampula' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Paul Banda
9 years ago

Number 4 you are as stupid as mucus. Bwanji osakamba zanzeru. VC 10 yake iti ukunena iweyo? If you know not, just close your toilet. Ukuti only two planes iwe ulinazo? Zaufiti basi.

Number 3…. Ukuti bola ku Mpoto? Kulinji? Tete is boomin ndi business. Kuli malonda kumeneku.

Number 2, winanso opusa iwe. Planes dont just land paliponse. Size ya Q400 cant land pa Mzuzu. Wamva?

Ndiza
Ndiza
9 years ago

When are you starting Nairobi route?

Akungolonje
Akungolonje
9 years ago

Kamuzu Int. Airportyo mukonzenso. Mumatichititsa manyazi kwambiri kwa amzathu omwe timakwerea nawo ndege za Kenya Airways, Ethiopian, tikamatsika pamenepo. Usiku timagetsi ngati ka koloboyi ka mzimayi wogulitsa kanyenya usiku kaja amaika mkatoni yokutidwa ndi plastic paper ya white. Taikaniko magetsi olongpsoka chonde. Magetsi a Kalozera wa ndege potela kukongola kuposa magetsi a mabuilding, zimudzi ndiye nyanyi, zomvetsa chisoni. Pitani pompa pa Kenneth Kaunda, Jommo Kenyatta kwatalika kuti mukaphunzireko za maonekedwe a Airport chonde.

Akungolonje
Akungolonje
9 years ago

Kamuzu Int. Airportyo mukonzenso. Mumatichitsa manyazi kwambiri kwa amzathu omwe timakwerea nawo ndege za Kenya Airways, Ethiopian, tikamatsika pamenepo. Usiku timagetsi ngati ka koloboyi ka mzimayi wogulitsa kanyenya usiku kaja amaika mkatoni yokutidwa ndi plastic paper ya white. Taikaniko magetsi olongpsoka chonde. Magetsi a Kalozera wa ndege potela kukongola kuposa magetsi a mabuilding, zimudzi ndiye nyanyi, zomvetsa chisoni. Pitani pompa pa Kenneth Kaunda, Jommo Kenyatta kwatalika kuti mukaphunzireko za maonekedwe a Airport chonde.

Akungolonje
Akungolonje
9 years ago

We need affordable local flights here in Malawi. Mulanje-Blantyre-Zomba-Mangochi-LL-Kasungu- Mzuzu. Dont just consider international ones and yet you describe your airline as Malawian- which malawians go outside weekly. Can a usipa business man/woman, a common civil servant fly to Tete and Nampula weekly? Bulshit!

Mbolo Sidwala
Mbolo Sidwala
9 years ago

Ndege ziwiri basi? Osakonzetsa ma VC 10 aja bwanji kuti aziyenda domestically?

Mathanyula
Mathanyula
9 years ago

uchisilu basi kulichani ku tete ndiye Bola ku karonga

MAKONOKAYA
9 years ago

STUPID DEVELOPMENT HOW AND WHY TO NAMPULA / TETE NOT OTHER PARTS OF MALAWI ???

nikisi
9 years ago

When will flights to Mzuzu and Karonga the dead north start?

Read previous post:
CounterJab: North Malawi wants federalism? Be daredevils, go for independence

Selling the idea of changing the way Malawi is governed it is not an easy task. Leading public intellectual Edge...

Close