Email a copy of 'Malawian husband kills himself in South Africa, injures ‘cheating’ wife and baby' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawian husband kills himself in South Africa, injures ‘cheating’ wife and baby' to a friend
Rising commodity prices; general economic malaise; and growing dictatorial tendencies by the late president Bingu wa Mutharika had led to...
Anthu mulu ku malawi, article iyi ikusowa information yambili mmene wafela Daudi ndiponso siyani kumunyoza Vic. nkhani zawo simukuzidziwa bwino. ndi ku Joburg kuno. mukanadziwa sibwezi mukutukwana.RIP Daudi and Quick recovery to Vic and the baby. – See more at:
chindele chakufikapo
DAUDI MWASINGA, wafa imfa yopweteka kwambiri. mulungu yekha ndi amene akudziwa chomwe chachitika
foolish man, killing himself because of a cheating wife? why not divorce her? Many serious women out there nanji naji joni, aaaaaaaaaaaaa very appetizing women. anyway that’s what he chose but guys let us not be this foolish.
Ichocho thats the power of anger guys lets think b4 doing zinazi you see kwao amadalira iyeyu komaso azimazi chonde wat do u want kumakhutila ndi chomwe chili mnja mwanu mo
Uyu Daudi Chipenjere Chipatu Mwasinga ndi mwana wa mu neighborhood yanga, Hangalawe Chilumba. Am grieved. Couldn’t they file for a divorce? Ndimva bwino. RIP bro, you have followed your dad and mum but too soon and in a bad way. Peace!
Ndiye wachibwenziyo adya katundu motakasuka tsopano..life!!
Chipatu Mwasinga tinali tonse ku Mzuzu Gov anali player wabwino RIP to wife enjoy mbolo zosiyana siyana palibe wokupinga pano
Onse akunyengana nawowo amusiya…..amuthawa akuyesa chani. LEHU
When u say 2 children, r u including the one he suspected not to be his?
But some men are extremely foolish eti? Suicide all because of mkazi? Can’t even begin to comprehend! Osangomtaya bwanji? And there are a lot of them. In dozens. In fact in hundreds! Amakoma chimtundu chani ameneyi? Kumbwambwana mapeto! Rest In Pieces!
Too bad indeed my brother from my home area! wanganya kwa uli Daudi up to that extent? may his soul rest in peace