Email a copy of 'Malawian is Africa’s Change Maker of the year: ‘Empower the youth’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawian is Africa’s Change Maker of the year: ‘Empower the youth’' to a friend
A 19 year-old third year Vitumbiko Thindwa, who is pursuing a bachelor of arts degree in education language, was elected ...
Powell is Powell and James is James. Mmimba ndi mchipala. Congratulations. Tikufuna ntchito za manja ako zichitirenso umboni kumudzi kuno. Keep on inspiring your fellow young men. Those of you that are writing against Powell, inuyo kwanu kulibe zidakwa? Be careful with what you comment on this page
Powell m’bale wako angomwa kuno ndikupwala…..at least iwe ukupanga za nzeru!
Great malawian
pa zabwino ma comment kuti ziii. koma zikakhala za ndale kapena chigololo ndiye 199 comments. this just shows what we prioritise are as a nation.
anyway, olo tisakudziwapo chilichonse cha iwe, zomwe umachita olo komwe mumapatsilana awardiyo, well done youngster. keep it up.
Wawa Muje! Iwe Ndiye munthu osati zinazi. Ukamuuze brother wako Powell asamangomwa mowa ngati nsomba apa. Shit