Email a copy of 'Malawians heading back to South Africa were being trafficked' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawians heading back to South Africa were being trafficked' to a friend
After the success of its social weekends at the Polytechnic, TNM Smart Data invades Mzuzu University (MZUNI) for Social Weekend for...
Welcom 2ur original home malawi land of peace just welcom this situation kukakhala bata u wil go,provided u stil alive.
Kodi chinthu chimene chapha anthu ambili ndiichiti, Zenofobiya kapena Aids? Bwanji anthu sakusintha khalidwe[kusaiopa] Aids yo? Ndiye asebwelele ku moyo wantofotofo ngakhale kuli zowophya? Ndiye wina wake asamanamize anthu atakhuta tiakachaso taketo kumanena kuti azaphunzitsa/kulemba anthu ntchito. Adzaapatsa ndalama zingati pamwezi zoti mpaka kugula malata zidina ndikumanga nyumba? Abale inu koma amalawi ena kuzipopa. KuJoni kwatukula miyoyo ya amalawi ambili. Anthu ambili asiya kugona munyumba zamaudzu. Tulo tabwino chifukwa cha Joni imene. Kodi anthu amene afa ndi chivomelezi ku Nepal ndi Zenifobiya imeneyo? Olo ukafuna uchi wokoma, umalumidwabe ndi njuchi. Aliyense ayandele yake. Nthawi yikakwana Yakwanabasi.
Sazaonekanso munthu yemwe angakwanise ku bwenzelesa dziko mmalo mwake chifukwa kunalembedwa kale tsono dzikuchitikaz nzongo kwanilitsa malembo,abale ndi alongo chonde ndimveseni ndimveseni inosinthawi yolimbana ndikulozana zala ayi koma ndinthawi yozikonzesela moyo wanu mlaliki akut zones nzachabe ndizinthu zongosausa mtima.:(:/;(odala iye amene amve mawuwa ndikuwa gwiritsa ntchito mtendele ndimadaliso zikhale kwa iye :>:DMULUNGU AKHALENANU(filimon Amos wa mtukula)
Kulibwino kupita ku s.a. Kusiyana ndikumagula ndege yoti wina azinjoya kuchoka ku misonkho yake nkumasauka shit!
Guys Zigianizileni Anzanu Tikufewa Konkuno Ku Malawi
Malawi government is too corrupt and biased.It only employs their sons and relatives thats why we accept to die in South Africa.
U
Asiyeni apite aliyense ali ndi imfa yake, ena sakafa than kuti tinene kuti tiwasamala koma osakwaniritsa. Pamalawi kuti umgaire mzako chinthu ndekuti pafa mzungu. Let them go.
Malawi government must agree that we suffering to the world
Akalawa voloso sakusika!