Email a copy of 'Malawians in South Africa mobilise support for flood victims' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawians in South Africa mobilise support for flood victims' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) and leader of opposition Lazarus Chakwera on Saturday visited over 200 flood victims in Chilobwe Township and donated...
Lets sin together as a malawian no matter wich side of malawi u cum from bt wi ar al Nyasaland.An my corcen is people dey ar close to de donation dat wil cuming to de country from different country,plz is not time to budget wat car u wil buy or wat expensive xul u wil send ur child with donation money try an feel if it was ur family beeng afected with dis flooding how cud u feel as a human being born from amother,so Amalawi amene muli boma plz sithawi ya corrumption ndi thawi yoti muthandize dose who ar… Read more »
Blessed is the hand that giveth May God bless You guys. Inu mukunyoza kuti zachepa mwachitapo chani? POsankhana mitundu, we are all Malawians bretheren Kamuzu anatiuza kuti tonse ndife a Malawi, zonyozana mitundu izi will not take us anywhere. Mchifukwa chake alomwe onse atitengera mavuto posankha wakwao mosayanganira kuti mchimwene wake anatizunza bwanji. mukamalimbikira zosankhana mitundu anthu amasiya kuganiza bwino nzeru zao zimayangana mtundu. Ndapota nanu tiyeni tivomerezane kuti tonse ndi amalawi oposankha mtsogoleri 2019 tidzasankha on merit. God Bless Malawi and its People Amen!
#NZIKA, IF U LVE IN SOUTH AFRICA, THERE IS A PHONE NUMBER IN THE STORY WHICH YOU CAN CALL AND YOU WILL BE TOLD WHOM TO CONTACT IN THE AREA YOU LIVE. YOU ARE NOT SECLUDED
aNAC dola munapatsa mabungwe la Mathanyula ndi Nkhwangwa yake tengani gulilani makondomu apite kwa anzathu akukhala m’mathenti kamba ka madzi osefukila chifukwa m’matentimo AZINGOPWALANA mapuleni EDZI inkela ntsogolo. Iyi ndi ngamo a NAC…………On a rather serious note, to you all brandishing your FWE FWE FWE misplaced hatred for Tumbukas. For once why don’t you accept the superiority of my PEOPLE over your slumbering central and southern region tribes. Malawian history testifies openly that Northerners are far more civilized than you people. So, swallow your pomp and pride and give us the respect we deserve for we have contributed much more… Read more »
Shut up! Galu iwe, ikufuna anthu ayabe kudana ndi kuyamba chipolowe chifukwa za nosense ukukambazo zo sankha tribes. Fotseki. Osayambitsa chipolowe. Tonse ndife a malawi, ti thandizane pamene pali mavuto..
Ambiri mwa inu aphwanga ndakuwonani nanunso mukufunika chithandizo dziko laeni mukukhalalo. Tangobweranikoni, kapena tisonkhe pang’onopang’ono tizakutengeni. How can the multitude of you raise a meagre 1300 Rands towards a colossal mishappening that has begotten us?
Thanks
this is a good project, lets continue the good work
Dalitso, you are wrong, the department has always had poyambira as govt but cannot reach out to everyone this is why they are appealing to well wishers, learn to give and you will be blessed.
Giving a hand to someone who is in problem it’s a blessings May God bless you guys for your contribution
chonde zisalowe manyado kumeneko coz enanu mwayima ngati zikukusangalatsani