Email a copy of 'Malawians pray for flood victims' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

13 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Arthur G.M. Mtambo
9 years ago

MWAONONGANSO NDALAMA ZIJA, KUMATENGA ANTHU KUTALI AZIBAMBO, AZIMAI, ANYAMATA, ATSIKANA, NDI AMAKWAWA KUPITA KU BLANTYRE, OSATENGA AKU BLANTYRE KOKO, BASI KUFUNA KUBA NDALAMA KUZAMATI KUTI TINALIPILILA MAGALIMOTO, CHADYA NDI ZINA NDI ZINA ZA WANTHU OBWERA, NDI MALAWATSE MUKATI.
MWABA ZOCHULUKA ENA OVUTIKA ALIBE CHILICHOSE ——- HA TSOKA ILO

Chief
Chief
9 years ago

Kodi agalu inu, kumapepheloko msalu zachipani zimakataniko?komstu mudya michenga chaka chino.makamaka ku mwera kwa lomweko.mutong’ola chili pa msalucho.

ben wa Ben
ben wa Ben
9 years ago

Unity for the good purpose

aunt so
aunt so
9 years ago

Ovutika ndi owonela eni ake akuziwana

ayu
ayu
9 years ago

it was only last month you went to pray to your god for rains, today you’re praying to him/her(especially catholics to mary) to stop the same rains, are you ok in your minds?? didn’t you ask your god for an amount of the rains at the first place?? there are floods, storms etc in America and all over the world, have you ever heard of Obama organising prayers to god?? for what?? this is waste of money, time and energy. the lost resources could have been used for more productive course, eg civic educating citizens on need to take care… Read more »

Jebison Slindine Nyoni
Jebison Slindine Nyoni
9 years ago
Reply to  ayu

My understanding was that the prayers were convened to remember those that perished in the floods and not necessarily to pray for God’s intervention on the incessant rains. So before criticizing read and re-read.

losco
9 years ago

OChakwera odathawa pa guwa lansembe odasiya kupemphera.Pano angotsilira Apm.

Patriot
Patriot
9 years ago

Kikikikiki nthawi yonseyi anali kuti awa. anthu afa uko mukubwera pano. Kutoleranso ka meagre 600 kwacha, kachani?
Next time osazawasiya asilamu kupemphelera mvuala ayi, mwaonatu, mvula yake ikumabwera ya boko haram.

Zanga Phee!
Zanga Phee!
9 years ago

Does this mean UDF never participated the event yo!signs and symptoms when the party is going to die no wonder,See MY Name Name.

mlomwe wosapusisidwa
9 years ago

Bambo tonde wadula simumadziwa kuti UDF inamezedwa ndi DPP? Ifetu tinadziwa kale komano kuti mumufunse Atupele ndi anzakw omwe akudya nawo za DPP akuuzani kuti izi UDF idakalipo adzakuuzani choncho chifukwa iwonso sakudziwa komano atsekuka mask kutsogolo kuno nambala ya aphungu 14 yomwe anawina ija ikafika pa atatu.

Manyeretsa
Manyeretsa
9 years ago

APM umakhwana, apastseni moni mbusa otembeleledwayu!!

chakwanuleka
chakwanuleka
9 years ago
Reply to  Manyeretsa

Take is easy. Dont judge him too early. He may laugh last.

Read previous post:
Malawi coaches in national wide player identification duty

Football Association of Malawi (FAM) has announced that national team coaches will start conducting countrywide training aiming at identifying new...

Close