Email a copy of 'Malawi's ex president Joyce Banda to return home this Saturday' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi's ex president Joyce Banda to return home this Saturday' to a friend
Innocent Chitimbe popularly known as D-7 “Namatcheni” has expressed optimism on winning his first award. Chitimbe’s comments follow his Nyasa...
Let her come back, ine ndikudabwa anthu akuti anatithawa, anakuthawani kuti chani poti anakusiyani ndi president, she didnt go away as president but as former president, so whether she remained here or not i dont see any significant thing she would have done to malawians as there is a sitting president running the afairs of the nation. Mukamati anakuthawani ndiye kuti mumamufunabe ndipo munamusowa kkkkkkkkkk. As for za cashgate mmmmm zisiyeni muonanso, for her to make such a decision kuti azibwera she has done enough consultations and she knows her position very well, tisanamizanepo apa ndi pa nyasaland pano, ngati… Read more »
Abale maiwatu kuno nkwawo..mthengo mudalaka njoka..mau akulu adatero..mai welcome home..ngakhale pa banja pamakhala mwana wina olowerera..koma amayenera kuzabwerera tsiku lina..a APM etc nawo anali moyenda mommo ngati inu anabwerako..lero si awa ndi a pulezidenti lero..kkkkkkktinakusowani ndi ti nyhabwala tanu tija..kkkkk
Lets test the accusations then
Kaya adzabwera, kaya sadzabwera trilibe naye ntchito, anatibera akugwira ndende yozimanga yekha.Woipa amathawa yekha. Ife zathu zili bwino bola moyo kwanu mkwanu
Lucius Banda once sang that UDF has failed us BUT going back to MCP won’t be such an honorable thing to do. IT’S ALSO VERY TRUE TODAY! DPP HAS MISERABLY FAILED US BUT GOING BACK TO THE DEAD PP WILL BE SUCH A DAMN THING TO DO!!!!
Iwe Andekuche usatinyanse ndi ambuyako uyenda ngati bakha aja!
Olo asadzabwerenso tilibe nawo ntchito ife!
Kodi uli nacho chimanga choti udzachitirenso campaign yako ya ukhansala yopepera ija Chaka cha mawa?
PR gimmick. Mark my words come Friday we will be told she has failed to jet in because of other engagements abroad. Cashgate Coward. She was bold enough to steal our money but but very coward to jet home. Stop this ‘JB is coming back home’ noise. Spare us this nonsense.
NO TIME FOR THESE OLD WOODS
PLEASE !!
YOUTHS WAKE-UP YOUR TOMORROW IS NOW !!
THIS IS 21ST CENTURY !!
WE NEED VISIONARY LEADERS
LIKE BUSHIRI PERIOD !!
Ng’ombe yayimuna yakanika kukoka ngolo!!! Mbwelani ndithu mayi mudzawongolele dziko lidachita ngozi
Kkkkkkkkkk, yokhayokha ng’ombe yakaomba mtengo….ikukanika kunyamuka…..Wena akuomberabe mmanja….ambuye bwerani mudzangolithira madzi dzikoli.
The mere fact you’ve in the news over cashgate you coming onto the scene we feel JB offers the best relief to the DPP that has been feasting on Callista leadership crumbs the journey to 2019 elections will centre around JB the court circus will draw away the nation’s close scrutiny on the DPP economic vampires the DPP leeches will find a common target which offer a cover for their criminal sycophantic operations around APM sorry JB you’re the soap for a DPP shower the heavens will fall on you these deafmutes won’t entertain international protestations on your behalf Callista… Read more »