Email a copy of 'Malawi’s internet tax slammed: ‘Retrogressing, anti-democratic’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

71 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chamazaza
Chamazaza
8 years ago

I commend the government in looking for ways to increase our tax base. However, economic prudence needs to be applied, a wholesale application of of some fiscal measures only serves to further marginalise the rural masses who unfortunately account for more than 80% of our nation. For example, Australia in its 2015-16 budget for the first time just introduced its on-line taxes but again only have applied it to goods purchased via internet to a certain capped value. This is what I call prudence, knowing what a country needs, using the resources wisely and then injecting it back into society.… Read more »

Prof Jon Diana
Prof Jon Diana
8 years ago

The so-called undeserving DCs can as well be retired.I’m told someone was high-jumped from P7 to P3.Ironically, the highest paper she has, so I’m fed, is an MSCE! Our 28-district country cannot afford the luxurious excess DCs.Hon. Gowelo, work some miracle here.

sniper
8 years ago

inu a dpp mwapwala anu enafe tikupanga xul mukuona ngat research tizipanga bwanj nd internet yodula? kuzolowera facebook ya ulere? …ts nt abt political parties koma logic…alomwe odya anyan inu!!!!

winiwa
winiwa
8 years ago

MCP ndi a goodall Gondwe waulesi ndani? Inu ntchito attacking,up to now, sitinamvebe mfundo zanu, bola awa zawo tamva.mukatero mwati inu ndalama zoyendetsera boma mudzatenga kuti? Tax makes Government move! unless you give another way. koma zoti a Malawi akhale akapolo a azungu, chifukwa chopempha?mukhala ku Opposition konko mpaka mukalambe inu ,sure!

LACKSON
LACKSON
8 years ago

Kodi kani ku MCP wanzaru anali kamuzu yekha? nchifukwa chake I will love KAMUZU BANDA forever! and hate those who are ruining MCP now! and I know, they are the ones who are making kamuzu unpopular with their behaviors, kupanda nzeru, kulongolola mpaka nseru zinthu zopanda pake. Ngati kamuzu manged to run smoothly Malawi, by collecting Tax from everybody, without donor money. People were paying for their children education… and nthawi imene yija a Malawi ambiri akungolima. lero a Malawi atukuka akalephere kupereka 10% ku dziko lawo? ndichifukwa mukumapusitsa anthu sukulu za ulele, akalandilenso phala???????? kuchipatala ulele?? asapereke 10kwacha pa… Read more »

HANANIA
HANANIA
8 years ago

mbuli ya mzimayi. zoti ndi mtsogoleri wachinyamata,akudziwa yekha.MMutu mudamata.Choncho MCP mudzalowe Mmboma? ndakayika.mudzationongera dziko,no Mahala. simunanadziwebe Government is Bussiness? it gives back to the People what it collects from TAX? kani zinazi mumangoziyamba?mxii! mbola

wenena
wenena
8 years ago

Kupanga kuti ma phone azidulidwa % ku ma SMS ndi nzeru, mmalawi amene ali ndi phone Malawi muno wayenera kudula msonkho. asamangozolowera za ulere. Iwe Juliana, kapeze ndalama zaulere uzilandiritsatu.

Namoyo
Namoyo
8 years ago

Tamanenaninso za nzeru zoti Boma lichite ngati mukuti za anzanu nzaulesi!

zaoneka sizi
zaoneka sizi
8 years ago

most of them in the parliament, amamgoyenda ndi ma laptop osadziwa how technology work= ma secretary awo ndomwe amadziwa zocita, olo kutsegula email yao yomwe-nde za intrenet awa ndi anta

frazer
frazer
8 years ago

eish! At the time of buying a fon theres tax, buying credit tax and we shud also pay tax at the time of using

eeee guys this is killing us

Read previous post:
Malawi Savings Bank in contempt of court over Mulli assets sale

Mulli Brothers Limited (MBL) Holdings Limited claims Malawi Savings Bank is in contempt of court for advertising the properties of...

Close