The guy behind the article was at state house and from the clear look of things ,DPP and PP are all evil period
I love Malawi
6 years ago
Steve Nhlane khala chete usatibowe ndimfundo zako zofoirazi.aunt Joy had enough time to probe the mighty Dpp of any wrong doing during her 2year stay at capital hill.The reason she was quite is simple,;she found everything in place.ndiye pano muli ng’weng’weng’we chani.let the courts prove her innocence period!!!!!!!
Politics aside the article raises legit issues. how is it that of the 2 cashgates (the one that took place during DPP’s watch 2009-2014 and the 2013-2014 during amayi’s watch), only the latter has been prosecuted so far? It certainly reeks of double standards. Amayi might have a case to answer and she should but those responsible for the theft from 2009 also ought to be brought to justice. Just being a patriotic Nyasalandian
nsanai kugwe
6 years ago
tilley anadyapo zake. kafukufuku, ma komishoni thoo kodoi nde kuti palibe wokhoza kapena maina a mabwana a ma degree wa ma phd amaba nawowa ali pa list nde mukufuna wina odzacotsa mainawa kuti milandu iyambike?kodi mamuna wa ku PHALOMBE anali KEN LIPENGA monga sakudziwapo kanthu? analitu wa fanansi, nanga ka boyi ka JB SOSITENI GUWENGWE kanangolemera miyezi 5yokha kuti kodi salale yakeyo itiyo???????????
no wonder we are called a country that is FEASTING ON AID MONEY.
Natty Prince
6 years ago
Steve walemba momveka ndikudikila Ma kometi a makadeti.Pa malawi palibe chilungamo munasakha dala mbala zibani nthawi idzafika.