Email a copy of 'Malunga now wants to challenge Chamangwana on Wanderers club hot seat' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malunga now wants to challenge Chamangwana on Wanderers club hot seat' to a friend
If there are countries where people pray a lot, then Malawi must be among the top ten. Hardly do we...
Vuto siiye koma kochokera man kkkkk
DONT CONTEST YONA TO AVOID EMBARRASSMENTS, YOU KNOW FOR SURE THAT YOU CANT UNSEAT CHAMANGWANA,THE CHAIRMAN IS SUPPOSED TO COMMUNICATE IN BOTH CHICHEWA AND ENGLISH FLUENTLY CAN YOU MANAGE?
Kkkkkkkkk neba ma electon avuta kkkkkkk
Thats a set up by Chamangwana’s camp……for sure Yona is going to change his mind at the eleventh hour so that George could go un opposed……ine namanya kaleeee.
Nthawi yanu aYona kunyerere yatha,kuvomereza nkofunika.Ingokhalani sapota wamba basi.
HIIIIIIII KOMA ZINA UKAONA KAMBA ANGA MWALA
AYona osamadzipopa pamene mulibe anthu okusapotani kodi munthu umazivotela wekha?Taunani mwagwa nawo game kkkkkkkkkkk haha
KkkkkkKkkk koma zinazi kkkkkkkk
Ayona musatiseketse, u chair wa team umasiyana ndi kukhala Chair wamumsika , do you have intellectual expertise to run a team like Mighty Be forward professionally . Osamadzikwata ndi chala mwamva kkkkkkkkkkkk
VUTO LOMATENGA ZINTHU ZAGULU NGATI ZA MU NYUMBA MWATHU!!