Email a copy of 'Mangochi Councillors in a racket: Malawi Police arrest two' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mangochi Councillors in a racket: Malawi Police arrest two' to a friend
Enlightened Christian Gathering (ECG) leader, Prophet Shepherd Bushiri, on Tuesday gave out over 3 000 bags of maize to people...
This only shows financial systems are weak at Mangochi District council. Investigate all directors because by allowing such malpractices it means they also had their share in the transactions.
Awa ndi atumbuka omwe anasamukira ku Nsaka ndi ku Nkope. Kuba atumbuka
Abolish councilors. They are not necessary but a waste of resources that should go the poor Malawians.
mubwerenso ku mandimba ward ku namwera anthu kulephera kupeza chimanga ku admarc iyeyo atazembesa kuwagulitsa ma vendor. ma councellor awa ndithu satithandiza
Kodi Mr OC Kachikuwo, inu nkhani yani ya 400million ili pati?
ife ku bangwe sitinamusankhe Isaac jomo chifukwa timaopa zomwezo.
Nelson Salade is a councillor and ndi wa katapila. How tinamusankha is a mystery. We hear Chairman wa District council is also involved. Komanso investigate Chiwaya. He is building a multi million filling station which will be one of the best in the whole Mangochi district. Where is he getting the money from
mbava zakumwera in the name of councillors!!!!
A D C, ndi team yawo alephera nchito ndipo a mangidwe makamaka a finance.
A DC ndi staff yawo achosedwe nchito alephera