Email a copy of 'Mayaya accuses Judiciary, Executive for interfering with legislature' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

43 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mbuli
Mbuli
8 years ago

I thought the speaker by acting on the Muyaya petition from a member outside the august house to invoke section 65 made a decision amenable for judicial review or am I lost on the whole issue? How is it academic then learned men? I dont think the honourable court can embarass itself by granting leave for judicial review on unmerited case. Let’s just wait. Funny enough, who will act for speaker in this scenario? Is it not the same Attorney General whose advice to the speaker on the same issue, the speaker chose to ignore after acting on it by… Read more »

Moni
Moni
8 years ago

Koma mwafikapotu a Billy Mayaya podzimva kuzindikira kwambiri, mpaka kunyoza amabwalo amilandu chifukwa choti chigamulo chawo sichinakukomereni? Eeish, koma UDF mumaidadi kosakugonetsani tulo ndithu. Mwayiwala kuti ndi inu nomwe motsogozedwa ndi anzanu a Mwakasungura mumakagona ku parliament kuletsa masipikila malemu a Munyenyembe ndinso a Chimango kuti asayerekeze kuthamangitsa aphungu monga a Chimunthu Banda, a Joyce Banda, a Ken Lipenga, a P. Kaliati, a H. Musa, G. Chaponda, a Uladi Musa, a Yusufu Mwawa, a Yunusu Musa, a Kaphuka, a S. Maulidi, a Katsonga, a Manyzo, a J. Musa ndi ena ambiri omwe anatuluka UDF mkulowa DPP? Si inu nomwe ndi… Read more »

kantengo kakawisi
8 years ago

Galu wa munthu ameneyu akhaula, munali anthu muno ofunira anzao zoipa, Kodiso mayayayu analikuti nthawi ya Bingu, zipwisi zimenezi sankapwisa nthawi ijai Bingu ataisiya udf chipani chomwe chinamuika panpando , kodi iwe Mayaya unali kuti , kapena umasenza matumba ku juberg ndepano ufunuchenjerere pa yellow mmmmhh ukunama ase uyisova npaka uwonda nayo , ngati mufuna kutchuka ndesipa udf , mupanga manyaz ndiposo amene akukutumawo adziwika kale and ts recorded,watch out

KANDAWE
KANDAWE
8 years ago

I SALUTE U JELBIN @# 18. JUDICIARY IN MALAWI IS THE ONLY ARM OF GVT THAT DOES NOT RESPECT CONSTUTIONAL POWERS OF LEGISLATURE (PARLIAMENT)

manganya
manganya
8 years ago

Koma amayaya China ndi China ndinu munthu onyasa andakuone tsetsani lero ndipo mwatha kwambili. Mukudwalatu inu ndioo vomelezani Mani.

Chief Critic
8 years ago

Mayaya wa mcp nkhope ngati mfiti. Where were u when Dpp mps ditched the party and joined PP?

mdk
mdk
8 years ago

Mr mayaya are you trying to to tell us that you never expected for this to happen?iwe umafuna azingotsatila izo ufuna iwe?it’s stupid of you to let your emotions lead you.anthu amasiya zipani zawo zenizeni not izi zosemazi mbuyomu unaonapo section 65 ikugwila ntchito?so what made you think it’s going to work pa zokakamizazi?we all know you support MCP.wait for your time bro izi zizingokuchedwetsani

POLICE BELL ndiyawulele
POLICE BELL ndiyawulele
8 years ago

Ngati jaji wake ndi Kapanda, basi nkhani palibe apa. Ameneyu sanganyoze UDF anamuyika pa ujaji ndi atcheya. Nkhani imeneyi yamwa madzi basi.

Chimulhakho cha
8 years ago

DPP, UDF and the judiciary ndiye mbutuma and you too who is saying that Mayaya ndi Mbutuma alongside your whole family are all fools and brutes.

Mugonapamuhanya
Mugonapamuhanya
8 years ago

That is why some of us have and will remain convinced that Malawi does not have activists. When DPP MPs ditched their party to follow JB’s PP, Mayaya was there and he clapped hands. When the PP’s Lutepos, Mphwiyos, and Kasambaras stole billions of tax payers’ money Mayaya was there and he clapped hands. Today, he is mobilizing people to demonstrate against the MK92bn audit querry that is being followed up by independent bodies. Today he wants to mobilize us to demonstrate about UDF MPs whom he thinks have dumped their party to join DPP. The matter is simply semantic… Read more »

Read previous post:
CARE Malawi winds up Nutrition Projects in Dowa and Kasungu

Communities in the two Central Region Districts of Kasungu and Dowa have hailed CARE Malawi for successfully winding up its...

Close