Email a copy of 'MBC fires Mungomo: Board finds him guilty over theft and forgery charges' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MadaJokhupesi
MadaJokhupesi
7 years ago

uyu mukuti Albert. Kuba anayambadi kalekale gologolo wachabe chabe. Mkuluwakenso Brian chimodzimodzi. Albert saziwa ntchito ta pang’ono amabisalira kwa anthu andale to protect him. MBC muyang’ane ma voucher akale you will find kuti ma trip a Albert ambiri anali a Fake. Tsiku lina ndinakumana naye mu corridor ku ntchito kuni akuti I’m chasing my cheque I have a trip to Lilongwe Ati ku meeting. Mbava yachabe chabe. pano pa MBC Ku Administration yathu pofunika Kusintha amangosainira zilizonse without veryfying. Ndalama zambiri zimatuluka chifukwa cha weak administration. UYU Simango yamukulira ntchito. Komatu Albert apite kuchitokosi.Finance yathunso is so weak. Staff must… Read more »

Afana Zedi
Afana Zedi
7 years ago

Koma kankhopeko kutuwa chonchi ngati kuti wazola sopo ya Maluwa kumaso? Kodi sangathe kugula ka Vaseline or ka Cocoa butter ndi ndalama zokubazo?

Moya
Moya
7 years ago

Going to Mangochi just to attend to a thief? The chairman of the board needs to be fired…if only Mutharika was like magafuli or any other president who understand the dire situation malawi is in…i cry for this generation they have rotten wrong models in leadership position

Mapwevupwevu
Mapwevupwevu
7 years ago

I have met Gloria and she has confided in me that she is regretting leaving her loving husband Ralph for Mungomo who lured her with stolen money.
Gloria waneneratu kuti mmene zilirimu adzingonyengetsa to maintain her life style!

Albert Mungomo
Albert Mungomo
7 years ago

Musalimbane ndi ine. I am not your size. I am well connected. Do not waste your tome talking no sense. I will soon be back and i will be back with a a bang.

Nyoooo!
Nyoooo!
7 years ago

Mumalembelanji ntchito mbavayo mukudziwa kale mbiri yake? Zisathele pompo izi koma imangidwe basi.

ndadabwa
7 years ago

a mungomo. chiwandatu chimenecho. mudzipempherere

njati
njati
7 years ago

Zamanyazi izi. Mpakana forging ma signature a anthu? Mlandu winansotu uwu. Chonchobe.. Koma asakalowe mchitokosi thanzi lawo will be compromised

Hoba
Hoba
7 years ago

Mummangise minty woipa ameneyi.Like sukulu alibe alowera kuti? Kukula konseko no first degree no wonder amabisalira my ndale.June mungomo anayamba kalekale.If you check me help ambiri amene wayenda that were fair like amagwirizana bro Mr Simango ku musainira ndikugawana zina.Achita zambiritu anyamata amenewa.

Banda
Banda
7 years ago

Welcome to Malawi where you can be fired from your government position for stealing the peoples money, then to be rehired into the same government department and do it again

Hopefully this will be the last that we see Mungomo
Sadly not likely

Alfred Minjo
Alfred Minjo
7 years ago
Reply to  Banda

This guy looks like a habitual and con thief……..

Nyoooo!
Nyoooo!
7 years ago
Reply to  Banda

No wonder the govt is full of thieves.

Read previous post:
Joyce Banda tells BPR:  ‘My legacy depends on how Malawians feel’

The Brown Political Review (BPR) had an exclusive interview with Dr. Joyce Banda who served as the first female president...

Close