Email a copy of 'MCP boost! Chakwera welcomes back Gwengwe, Kayembe, Zulu, Kalazi Mbewe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP boost! Chakwera welcomes back Gwengwe, Kayembe, Zulu, Kalazi Mbewe' to a friend
Egyptian Ambassador Maher El-Adawy has hailed the cooperation between Malawi and Egypt, saying the diplomatic relations are on track to...
Time for MCP is over dead & buried
MCP idaliko kale izi ndi masewera palibe chikuthandiza ku parliament ntchito yawo ku songoneza
uku ndiye timati kupepela povota munatipusitsa mavoti tidagawana kupanda zitsilu ngati inu okomedwa bwezi tilipati?a kawila mzimu wawo ugone mu mtendele anthu oipa inu oyendayenda,asamva nkukhu,zitsilu,akabwelebwele, mufuna muzatitape mkamwa
A WAKE UP CALL TO MCP !!
PLEASE INTESIFY YOUR .MEETINGS TO THE NORTH AND SOUTH !!
LOCAL PEOPLE NEED TO SEE AND HEAR FROM YOU MUCH MORE THAN BEFORE !!
DONT GIVE THESE PEOPLE A SECOND CHANCE TO STEAL YOUR VOTE !!
PLEASE ! PLEASE !!
mwanayo mulandileni sanaphe munthu
Nga nga nga pambuyo pa Chipani ndi Boma; sorry ndinaiwala chifukwa chozolowera mu zaka 31. Nga nga nga pambuyo pa Kamuzu sorry again!
Na ngati ziwirizi zatsowa ndiye kuti chipanichi chinatha basi; palibenso zoti chingazawine popanda anthu a kumwera ngakhale a Ku mpoto ndi pakati ataphatikizana.
MCP be very careful…. MCP does not need these recycled young men. It is these young men that want to use the MCP to reclaim their positions of MP. all what they will do is to cause instability in the areas they lost in the name of PP or DPP. These people have no constituencies as they claim because those areas have MCP MPs already. Why do you need them? they will not bring anything to MCP apart from confusion. MCP should be focussing on expanding its reach abnd political footprint into they areas they have potential to grow, and… Read more »
No wonder a certain political party from the MTL BELT is spending sleepless nights with Dr. Lazarus Chakwera.
MCP 2019 boma!
Zazii umawona ngati pp inakawina so that u shd b vp unalemba m’madzi achule anawerenga