Email a copy of 'MCP district chairmen insists on Chakwera’s resignation' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Moses Makoko
Moses Makoko
7 years ago

Ma disitilikiti chalamani noooonse, zakuti zanu!

success
success
7 years ago

ndinawadziwa Bambo Foloma Mwale Muchaka Cha 1985 ndikuphunzira ndi mwana wawo Sendman ku Ludzi Booarding School ku Mchinji. Pa nthawi imenyo mkuti ali kale District Chairman wa Mchinji. Patha zaka 31 kuchokera pamene ndinawadziwapo kufika pano. Analephera kulera ana awo chifukwa onse sukulu inawalephera moti pano amangokhala kumudzi kwawo kwa Kalulu ku Mchinji.Farm yawo Chimwanjiwa inawalepheranso.Pa moyo wawo Bambo Foloma mwale palibe chimene anapanga chimene chinawayendera.Ngati mkotheka mukhale pansi Bambo, MCP si inuyo ndife anthuamene tili eni ake.Inu mutayima apa ndi Dr Laz mungafanane mu nzeru,Ulemu kapena mu ukadawulo. Bwanaji osamavomera kuti nthawi yanu inatha. olo ma thalauza mwavalawo akuwoneku… Read more »

Maxson Mbendera (POISONED)
Maxson Mbendera (POISONED)
7 years ago

Mukamva sete ndizo akunena ma chairman ndi Chatikha wawoyo. Kagwereni uyu mutichedwetsa Dr Laz ndichiyembekezo cha malawi. 2019 kuchedwa ndikavotele Dr Laz Chakwera izi zatitopetsa tikufa ndi njala mulungu anakwiya tisayembekele mvula yabwino until DPP idzachoke m’boma, God is very furious with this governement.

Cash Gate
7 years ago

you old district chairpersons of mcp, for how long have you stayed on that position? mwaluzitsa zisankho zingati inuyo munthawi yanu? kodi maposition amenewa mukuona ngati ndi amuyaya? go to hell. mwatikwana kwabasi anthu olephera inu, mwaononga chipani chathu chomwe chinali champhamvu in all regions. sitikukufunani ife a mcp, anthu omvetsa chisoni inu, opanda nzeru, amanyangumvi.

Kenkkk
Kenkkk
7 years ago

Only stupid, ignorant and dpp bribed bootlicking so called mcp district chairmen can even think of bringing back tembo to lead mcp. Some of you mcp protesters don’t realise that by insisting on tembo to lead mcp, you are giving dpp a field day victory come 2019. They will use tembo’s past in the old mcp to easily defeat mcp. At the moment Laz and new mcp provides a formidable feared opposition to dpp, making dpp tremblie with uncertainty of any decisive winning in 2019. Tembo is easy meat for dpp and no wonder they are destabilising new mcp and… Read more »

Zuze
Zuze
7 years ago

So because you were a Chairman during Kamuzu, you want to be a Chairman now. kikiki

J. Cha
J. Cha
7 years ago

I hear some top officials in MCP are also secretly supporting Chatinkha Group. I feel this is just the beginning. Worse still, external forces may also have joined the battle. Put your house in order before the party loses its position in Malawi politics.

Khudze Mkuyabwe
Khudze Mkuyabwe
7 years ago

These old men are tired . We want a new MCP with new blood. Its been avery long time since I have been hearing the name Foloma Mwale. These old guards need to retire. We need new blood in MCP not these tainted with blood in their hands. Please accept your time is up. ASA Fotseki. MCP has to rebrand.

Chigumbuli
Chigumbuli
7 years ago

Chpani chakuvutani to run abwezereni eni ake a chipani. The Mpamba people of Nkhatabay kikikikiki.

jooo
jooo
7 years ago

if these people are not supporting Chakwera let them quit, leave MCP . or wait for convention, MCP will go for convention for sure let them campaign for that time not desturbing the party. we are geared for 2019

Read previous post:
Malawi President Mutharika claims: ‘I was hunted like criminal, survived 5 assassination attempts’

President Peter Mutharika has said the culture of hatred resulted in him being hunted like a criminal at the time...

Close