Email a copy of 'MCP executive reshuffle: Mwalwanda roped in, Jumbe demoted as Chimango is back' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

110 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chimwemwe
chimwemwe
8 years ago

mcp ichenjele ngati ikufuna kuti 2019 iwine. ppo hav lost trust in DPP coz thng r not working. should we hav hope that things will changa?. mapoliticians akumalawi amakonda dyela. akawona chipani chawo chaluza amathawako. zamanyazi!!!

kazeze
8 years ago

A Chakwera, tasinthani chipani chioneke truly national, not central regional. Muzaluzansotu mu 2019 mukazitengela chibwana. The party needs structural transformation, not superficial /cosmetic changes. Malawians still remember the bad sides of MCP, don’t be cheated they have forgotten, no, and don’t uncover those wrongs as they surely will sink you. MARK MY WORDS. You should almost be saying MCP is a changed party and show how it is a changed party. Ngati a Kamuzu analephera in the end it is because he did not see what the people were seeing in his administration, and you seem to be going in… Read more »

emmah
emmah
8 years ago

oona tilipo tiyenazoni

CURUPT CULPRIT
8 years ago

MCP is a party which cannot cope up with the modern ERA. How come they still hold on to the DICTATORIAL So called ‘Four Corner Stones’ which are absolutely “UNDEMOCRATIC” which if applied today, will inflinge human rights in many ways . Kodi ndani uyo obadwa mu ‘Democracy’ angasapote zaozo. They just talk of ‘Reform’ in papers but in reality its still like what was there in the 31 years. Do not forget, Atsogoleri ake ndi timilungu tosafuna kutsutsidwa. Uyu adatopa ndi chachikhumi ndiyenso paja amaoneka ngati abweretsa change koma…. kokoliko kwacha!! Tambala malilidwe ake ndi omwewo kaya wa Chimetere,… Read more »

clement
clement
8 years ago

We can’t waste our time to vote for mcp never.DPP is there to stay. Whatever you can say against the blues, we will be rallying behind them. Mcp stole alot of money but that time people didn’t know anything coz it was in the dark ages now everyone is awake that’s why you are saying fwifwifwi. We can’t accept mcp to rule Malawi again maybe other party

Chiheni
Chiheni
8 years ago

MCP nde chipani chachitikuko chodziwa kusamala nzika zake, Kamuzu adatimangira zinthu zambiri, kutsekula ma company ambirimbiri anthu nkumapeza zintchito,pano agalu a UDF,DPP,PP atangwanika kuzigulitsa, mikonono kuma state house zomwe adakumangirani Kamuzu mmamva bwanji mukamagonako zoti simudamange ndiinu? womanga ndamene mumunyozayo.Zifunseni nokha since 1994 UDF DPP PP adamangako nkutsekulira company zingati mdziko muno anthu nkumalowa ntchito?
Panbo zinthu zidasinth one party system inatha MCP onse amene amaiipitsa kupha anthu,kupanga nkhanza adathawako ndamene akutibera ma billion panowa chifukwa nthawi imeneyo sikunali kotheka kuba ndalama za boma

Nyovest
Nyovest
8 years ago

All those evil doers during MCP rule rebelled, walked out and form UDF,
MCP is now i CLEAN, white as snow, BAkili Muluzi was secretary general during those days nde muti chani

mulamu pelekani@gmail.com

The problem in Malawi is people can not accept changes or being dropped out. This is normal in every job and position in th whole world but not for Malawians. This is why they keep jumping from one party to another when they are left out or changed. And also thi i why there is cash gate. How can these people be serious political members. There is more to learn when it comes to politics. In Malawi politics is no to serve th nation but business. Unforunately. Look at Kachele. When he was dropped out he joined DDP thinking he… Read more »

Che Ngana
8 years ago

Heheeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee Eyi Eyi Eyi Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk Koma Mpakana Foloma Mwale Hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahaha Mamamamamamamama Mh!Where Is Samuel Kaphuka Here??Amene Mmatengeka Ndi Mcp Kumwera Kuno Mwazionatu??Atangoku Uzani Apa Zauchitsiru Za Zii.Ikanakhala Cabinet Mukanamva Bwanji.Mu NEC kumaikamo anthu oti olo “a” samatha kulemba koma chifukwa choti anakhalapo wa youth komanso waku central region.haaa kumvetsa chisoni.jumbe apilira sinanga by ya royalty and discipline za ziii.kummwera kuno ndiye musazataye nthawi yanu.ma rejects onse ku mmwera kuno akumajoina mcp kokausa sianthu oti angakuthandizeni.ati mgwirizano wa mcp ndi pp.mukagwera limodzi sure.

peter
peter
8 years ago

kodi mukunena za Makangala chifukwa chiyani? ife snthu akumwera taphuzira pa ulamuliro wa china. Munthalika kuti iwo hamaziwa chikhalidwe cha kuno kumwera. MCP ndi chipani chabwino. chopani chosaganitsa anthu.

Read previous post:
Kalonga’s JB cashgate link ‘hearsay evidence’: DPP says guilty plea milestone in pursuit of ‘big fishes’

Director of Public Prosecutions (DPP) Mary Kachale told High Court in Lilongwe during the conviction of former chief tourism officer...

Close