Email a copy of 'MCP MPs blast DPP poverty deniers: Mutharika told to mind the gap of super rich and poor in Malawi' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

68 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nico/nakhule/chiradzulu

number65 wanama koopysa ndipo ukulankhula ngati simukuona mmene anthu akuvutikila pitani pachioradzulu pomwepa apa mukaone mmene anthu akuvutikila .. kuthubwe kwa che H musa makawo anthu akuvutika osakhala masewela komatu tili ndi akuluakulu anthu ngati achina mwanamveka

rowland matemba
rowland matemba
8 years ago

mcp! mend the rift between chakwera and jumbe.jessie will you return to chanco after loosing 2019 elections?central region yonse yakwera ya jumbe.2019 jumbe for mcp torch bearer.

Uncle Ken
Uncle Ken
8 years ago

Dziko Ndi Choncho Asiyeni Ndi Nthawi Yawo Naye Mulungu Akazafuna Muzalamula

clement
clement
8 years ago

Mcp was supposed to be the first to mind the gap btwn rich and poor people but you completely failed for 31yrs just misusing donor funds. DPP is trying everything to rectify your mess for the fucken 31 yrs. You must shut up your mouths. DPP is there to stay more than 31yr and you will be crying forever.

Dr Mbewe
Dr Mbewe
8 years ago

Angulu party of DPP tchito zaje ndi kuba. K577 billion cashgate. Ndalama za madonor simuziona mpaka 2019 wooo. Mbava. Ifenso tikuti madonor asapeleke ndalama kudziko lino Chifukwa angoba a DPP

Nyau ya Lazaro
8 years ago

MCP created a big gap between super rich and the poor. It only focused on people to have three things: food, cloth, thatched houses. Today people can have more than these but they are still poor. Why???? Mcp denied people to own other things we see today: Tv, cars, vending, phones, minibuses, computers, internet, nyasatimes, freedom of expression etc. Muluzi did a good job to narrow the gap. The gap for 31yrs was so deep and grave that it requires another 31yrs to fill it. Mcp should pause and leave others to fill the gap it created. The south will… Read more »

Nyau Party
8 years ago

Kukadakhala kuti MCP (Nyau Party) inayendetsa bwino dzikoli (31yrs) with alot of donor funds, bwezi Malawi muno mulibe osauka lero. Koma ndalama zambiri mumathera mapwevupwevu. MCP inachita kugula ndege ya azimayi ndalama itasowa nazo chochita. (ndegeyo ili pa airwing). Ma delegates opita kunja amaposa 300. Munthu amene amamanga nyumba ya malata anali wa Theba basi. Nyumba zosathonya mumanena za udzu. Kodi Jessie unali usanabadwe? Foseki!!!!

Linwood de julius
8 years ago

masiku ano ndichoncho olemera azilemerese osauka kumulandilatu azingokukuta mano basi ukathamanga thamanga wina akulande kupitira ku america impishment ichitike basi

mapale
mapale
8 years ago

A female graduate has become a fool here showing that 120 delegates are on record without conducting a research. Look at the doctor. Kameraman wachita kukusiya kutali kuti wusaoneke ngati gule. Kodi Jessie are you still kuyang’anira dambwe la a gogo ako lija. Wachita bwino wabwera apa ndinakusowa. Chioneni mano ngati kang’wing’wi woti wavala kale zakugule kwake.taona anyamata uli nawo akuchita kuoneka bwinotu, matayi pho. Koma iwe uli mbuu. Garu iwe. Iwe ngati ungabwerer ku CHANCO after 5 years sabastical holiday ukasimba zoona kwa anzako monga Edge Kanyongolo amenenso akufuna kuti a Malawi achose lamulo la insulting laws kuti tizingophana… Read more »

andrew kambalame
andrew kambalame
8 years ago

MCP yaziwa liti kuti there is gap between the rich and poor. A chakwera tamangolalikirani zinazi siyirani a ndale apitilize. Nawo a Jessey Kabwira…. You critisise everything however we cannot trust you. Munthu ophunzira bwinobwino koma phokoso lokhalokha. Mukanakhala inu. Mwasiya ntchito yabwinobwino mumafuna chiyani ku ndale, si kuba komweko? Ndi chiyani chomwe mukufuna ku ndale. A chakwera, u bishop sizimakoma?

Read previous post:
Victor Mbewe burial Sunday at CI: Tributes pour in

Tributes have poured in on former governor of the Reserve Bank of Malawi (RBM), politician and entrepreneur, Victor Mbewe who...

Close